Email a copy of '390 Malawians arrive home from xenophobic South Africa' to a friend
Loading ...
Email a copy of '390 Malawians arrive home from xenophobic South Africa' to a friend
State President Professor Arthur Peter Mutharika on Monday met directors of the Brooklyn Institute in United States where among others he lobbied...
Njala mwaipeza abale to
Amene mwabwerako ndimoyo,prase God,zimene mwataya bola moyo muzapeza
Tsiku lina Mulungu azayankha
azizanga nonse amene mwafika from Jonz yamikani Mulungu ngati mwafika ndi moyo
Pepani kwambiri
It is both sad and happy moment to welcome our loved ones home.Indeed,what they went through break our hearts,but we must not over react to the extent of ruining our friendship between us and our brothers in South Africa that dated back to more than 100 years ago.At the same,we must realise the fact that in no time,you will find most of our brothers,will make the trips back to South Africa,because as it is,Malawi would not afford to give jobs to these young people due to its disorganized and corrupt economy which will take decades to stabilize.We must also not… Read more »
ENANU MUDANYANYA. MUDATHAWA KHASU.XOOL NNEEE! ZOVALA KUTOTENGERA MU SAKA BAG WA KU JONI KUMAKANGOMWA KACHASU WA UCHEMA. PANO MWABWERA PHAZI LIRI BARE NGATI MUKUOLOKA MTSINJE WA LINENGWE. NDALAMA IJA MUDAKONGOLA KUTI MUPANGIRE TRANSPORT NDIKUIFUNA. MUKAMACHOKA PA STADIUM MUNDIPEZA PA KHOMO PANU NDITAFIKA KALE. ULESI BASI
s.a citizens they pretend lyk savages ilipo dziko lomwe lingazdalire palokha?i hate this stupid south africans,togelther with their man with long pumpkin head and an2 ena samaganiza anzanu avutka ndpamene mukunyadla tkagule ma fon motchpa mukuyesa ndzosangala b serious somtymz kaduka bas mukuganiza ndtonse tngakhale mumaofes?
Boma takuthokozani kuti mwakanyamula abale athu.
Koma aboma tili odabwa kuti you are hiring buses from the very country that is caused us this pain. This is very suspicious. Komatu dziwani kuti ndi zimenezi zomwe zikubweretsa umphawi which is a cause of all these problems.
I am married to a malaiw it is very sad to me as a south african too let my husband go but he is scade i have to until this evil act is stop am very sad