Email a copy of '700,000 households in need food assistance: Malawi govt, WFP launches relief operation' to a friend
Loading ...
Email a copy of '700,000 households in need food assistance: Malawi govt, WFP launches relief operation' to a friend
Malawi Congress Party (MCP) spokesperson Jessie Kabwila has explained that her comments in relation to the controversial grants the National...
Punish him. He must cry in Lomwe.
Inu WFP kaya mmati ndani! Ife mungotiphunzitsa kalimidwe kabwino kuti tidzikolora zambiri, basi mwatitha! Chifukwa chaka chilichonse mudzingobweretsa chakudyachi.
Gogo nditanena kuti ndiwe mfiti ndiyesa sindilakwitsa, munthu wa mtundu wanji iwe ngati iwe ukudya kunyumba kwako usayankhule motumbwa. Ndikuuze kuti sibwino chilichonse kuchilowetsa udani kodi ukuganiza kuti zivute zitani APM angavutike? Wovutika ndi abale athu iye ndi wolemela kale.
20 years ago my village compound had 12 people including children, with enough fertile land to feed us all year round. Now there are a total of 38 people.
Isn’t it time we addressed the real problem in our country – uncontrolled population growth. Limited supply vs steeply growing demand for food (and everything really!).
Mwalakwisa kwambiri a WFP.Mukanamusiya pitala asove yekha kuti timukutumule bwino.Pamene apa azitama ngati akupeleka ndiyemwini pomwe boma lilibilethu chimanga.Tikufuna uyu pita alire mwachilomwe. A WFP tiganidzileni tithane ndi mbuli iyi once and for all.
Bungwe lathu!