Email a copy of 'ACB freezes Bophani bank account with his gratuity in it' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

42 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Chintengo
Chintengo
9 years ago

Amenewa anjatidwe kumene. Mbava zotha ntchito.

mr chimbwititi
mr chimbwititi
9 years ago

mumva ntedza, illovo kuti nong’onong’ono.agalu, anankalizi olumila ku nchira oipa ochinda anzao pakhongo ngati tombolombo. analikomkhwilo, zimbalangondo.

musekanji palibe kanu
musekanji palibe kanu
9 years ago

this is political persecution..how do you expect his family to survive..????ndale zolandana chuma ndizachikale kwambiri..kuchita nsanje ndi gratuity ya munthu inu a DPP??

vitumbiko mwakipuyi
vitumbiko mwakipuyi
9 years ago

Komadi a sam madula ali mugulu la kashigeti awa asatinamizepo apa,asaaa! Anayamba kuba kalekale mpaka kumanga mansion ku area 12 , asaa! Akukanthani Chauta mtheradi, mufa muzisiya muona! Ask Bingu, anatolera mkuzisiya wautali no return!

M23
M23
9 years ago

ACB, please freeze all late Bingu’s accounts and assets until they are fully investigated and cleared. I propose the government to set up a commission of inquiry to look into how the late president acquired his worth within a short period of time.

Yobe boo
Yobe boo
9 years ago

Corruption of Justice, away for Political persecution, for the survival of corrupt Politicians. Revenge at its best.

manford ngomah
9 years ago

njati osusana ndimalamulo ndiyo ntchito

Abiti Mtila
Abiti Mtila
9 years ago

Bophani paja unali body guard wa Lutepo eti?kikkkkkkkkk! Dyera amayi akupweteketsani! Iwo ali pheee akungodya Casgate yawo kunja! Amayi sanabe nawo iwo amangolandira. Wolandira ndiye kuti waba nawo ngati? Koma wotengayo eti???

Malawi Wa Dzana
Malawi Wa Dzana
9 years ago

And yet the same ACB is stalling Muluzi’s case with alot of funds, imagine MK1.7Bn and what’s your justification, ACB?

salimu
salimu
9 years ago

Number 22 you are an idiot Bophanis gratuity was not processed by Madula but the Police and there was nothing wrong. Nsanje basi why dont you investigate the MK400 million which has now come to more than MK 1 billion. Mtundu wosasamba always thinking you deserve better. Kodi kopanda Muluzi agologolo inu mukanalamula inu.

Read previous post:
TNM tunes up Mafco vibration band with musical equipment

Malawi’s premier mobile phone company, TNM has today donated musical equipment to Malawi Armed Forces College (MAFCO) Vibration Band worth...

Close