Email a copy of 'Angry father demands justice for son battling for life after Reds violence' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Angry father demands justice for son battling for life after Reds violence' to a friend
A tough punishment has been meted out on Red Lions for violent conduct during their Super League games against Surestream...
dzili busy kumenya macivilian m’malo mokateteza nyanja akutibera matanzaniayi!!!!!!!!!!!!!!!!!!!
Onsewo muwapititse ku Darfu,akakhale kutsogolo kwa nkhondo.akufuna nkhondo nang si kuno akungogona nkumangdya basi,DRC ikuwayembekeza amenewo,le them go there plz.Asasamba achabechabe,kuipa mtimaa choncho ngati ndinu adziko lina bwanji?Boko halam mukuiyambitsa poyereyera,oskalimbana kapena ndi Tanzania bwanji?
Ndakwiya nanu!!!!!
Kodi amaona off-side ndi ndani? Referee kapena linesman? Oyenera kumenyedwa anali ndani?
Stupid soldiers!alla naires,ur masa poes!
Ma solder apamalawi kuzikonda sichina chifukwa cha kusowa kwa mifuti kumalawi amaona ngati poti iwowo amagwila mifuti ndiye ndiwopambana agalu
What iz the role of soldiers in acountry?is it playing futbal ,singing at the stage ,drinking beer ,stealing &what beating innocent people when they want to win the matches in the local futbal pitch?nonsense ufailed to play ure trained game with tanzanians taking part of our land•but busy beating civilians shame on u•if this is what uwent to training for well done u are doing alot•but if not godforbid and what poor management cashgaters like u •organise ure own army league not this with locals or can we call boko harram for friendly with u or we do it ourselves… Read more »
Asilikali ayambitse league yawo, azimenyana okha okha.
geofry akuoneka kuti ndi mwana wabwino
bambo a geofry tengerani a sulom ndi anyamata a army onse ku khothi
palibe amene ali pamwamba pa lamulo
get well soon boy
suspend the team for the entire season not what you have done. Remember the concerns raised at SULOM AGM about having officials from military dominating SULOM official positions this is what you get injustice
kugwiritsa ntchito mphamvu in.a game of football ,ofunika tikuitanireni boko haram