Email a copy of 'Angry mob torch to death suspected thief in Mulanje' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

40 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Mrs Malawi
Mrs Malawi
8 years ago

Osamaotcha lone thief. Ofunika kuitchedwa ndi aja amabwera chigulu aja. Those ones din’t fear anybody and they kill guards and sometimes home owners. Samaopa kuthyola zitseko nkugwilira ana ndi mahi awo. Oba yekha ndiwamantha ndipo safuna anthu anve pomwe chigulu chimafuna mudzuke kumene kuti chikuzunzeni bwino. I wait for the day mbava 5 or 6 zobwera pachigulu cha 14 zitagwidwa nkuotchedwa mwina umbanda otereu ungachepe. They know no one can dare come out of their house to assist neighbours when attacked by 17 panga wielding thugs

Misheck sibande kaitano
Misheck sibande kaitano
8 years ago

KOMA OKUBA BLANKET AKUOTCHEDWA.WA CASH GATE 3THREE YEARS.MABILLION BILLION ADZIKO ANASOWA MAKHWALA NZIPATALA KULIBE,KWACHA IKUNGOGWA BOLA NDALAMA YAKU SYRIA.KOMA AMALAWI KUKHALA BUSY NDI NDIMUNTHU OBA BLANKET? KUSIYA WA CASHGATE?SHAME ON YOU!!!!!!!!!

Vitumbiko Ng'ambi
Vitumbiko Ng'ambi
8 years ago

Nchifukwa Stimalemera, Nzanu Abeko , Inu Mukupha, Iye Sanalakwise Chifukwa Ndi Thukuta Palokha Kuyenda Night

jet lee
jet lee
8 years ago

Apolice mukumabanso chifukwa anthu akutaya chikhulupiriro mwa inu

Genghis Khan
Genghis Khan
8 years ago

We’re all a bunch of hypocrites, we’re the same as that criminal who was murdered. Who gives us the right to kill and then claim to be religious, why do we even bother to go to church? Police do not even investigate these so called mob justice, why? Yes it is wrong to steal, I have been robbed a couple of times myself but I can never wish death on anybody, not because I’m holy, but because it is immoral and unlawful.

Zoona zake
Zoona zake
8 years ago

Wakubayo asabenso koma agwire ntchito molimbika ndi manja ake nagawane mphatso za kugwira ntchito kwake ndi iwo ali wosowa. Ephesians 4:28

Mjonanje
8 years ago

Wotchani wotchani kugula katundu ndalama zathukuta lako nkowawa, ndiye wina kungodzatenga basi, wotchani wotchani ndatero ine konstable. Akanganya amenewa azolowela

here we go again
here we go again
8 years ago

No arrests made by the police? The article is incomplete

Kunta
Kunta
8 years ago

Too bad

Himwemwe malepa manda
8 years ago

JUDGED

Read previous post:
Five arrested in Chikwawa over theft of medical drugs

Malawi police in the district of Chikwawa have arrested five people in connection to medical drugs stolen from Nyamithuthu Health...

Close