Another car sex scandal: Malawi police arrest married man and prostitute

A married man and a prostitute have ended up in police custody after being caught having a one-night stand in a car at Chez Mtemba International Night Club in the commercial capital Blantyre.sex-

Blantyre police patrolling officers caught 42-year-old Enock Chitewa and 28-year-old woman, Jane Nkamacha Monday at around 10pm making a whoopee in the backseat of a Toyota Corolla BLK 1389 that was parked outside the night club.

The incident happened just a day after Thokozani Maluwa- an internal auditor at Blantyre Water Board (BWB)- and Emma Peter were caught having a ‘car sex’ at Mwaiwathu Private Hospital parking lot.

Blantyre police Public Relations Officer, Elizabeth Divala said th two have since been charged with Idle and Disorderly under Section 180 of the Penal Code.

”Our officers on patrol noticed the car was shaking in a funny way and when checked, they found the two having sex,” said Divala.

Chitewa is a Bangwe Township resident but hails from Lundu village T/A Mabuka, Mulanje while Nkamacha is from Chiwembe in T/A Kapeni area, Blantyre.

They are expected to appear in court soon.

Follow and Subscribe Nyasa TV :

Please share this Article if you like Email This Post Email This Post

More From Nyasatimes

More From the World

214 thoughts on “Another car sex scandal: Malawi police arrest married man and prostitute”

 1. Junnie Chauluka says:

  Dziko likupita kt abale?

 2. masiku omaliza musadabwe

 3. Stone cold steve Austine says:

  Koma alomwe mwatani kodi ma rest house onsewa simukuwawona mtundu uwu ayi ndithu

 4. STAUB says:

  stop this bad behevior

 5. Ngwazi Matera Waku Mulanje says:

  sex?????? kma mukagonana mugalimoto nde chik imapasidwa ndalama??

 6. andy says:

  A londawo anangokhumbira basi bwanji nsanje chitani manyazi Ma gaurd nonse awuusiku

 7. Yabulu mwana says:

  Mupitenso ku mpanda wa Church ya Mai Sighn opposite ziboliboli madzulo from 7pm, mukapeza ambiri…apolosi akagwira anthu kumeneko amalandira K10 000 minmum…..haahaahhaaaa wa police wa pa nyasaland

 8. I mean banda says:

  Okay sex munda. Sex patchire. Is it only a crime in a car.where are these laws from..how is sex in a car falling under ” idle and disorderly” act. It is not unlawfulto be idle and it iisn’t unlawful to be disorderly or in normal..it is only when you act like that in public..hence we all can choose to be idle or disorderly in private places. Legally maiwathu car park is a private place therefore I think it is an invasion of privacy for the state to intrude into what occupants of a stationery vehicle are doing inside a vehicle in a private place. I am sure it is not illegal for consenting cabin crew to go into an aircraft packed at the airport and close the doors and have sex. The main word in this case is unfortunately ” car sex” and not ” public sex” ….do we need to légiste copulation in vehicles.bicycles.boats.aircraft.on internet . Gardens. Forest. Etc. No we should adopt the British law .just criminalize public sex and then know the meaning of public is ” presence of people whether in privaye house getting watched or in group sex in a hotel room it is public sex and sex in a public place where there no one to watch.witness isn’t public sex.public doesn’t mean a place privacy isn’t a place.

 9. mapasa says:

  Nokha mwati mkaziyo ndi Hule ndiye mumati angomupatsa ndalama osamuchinda , a polisi mwasowa zochita.

 10. Cydrick Mgunda says:

  Alekeni anthu achite zomwe akufuna. Monga inu simukudziwa kuti ku Rest house nkodula?

 11. Tipemhere kwambiri the devil is at work

 12. T Dn says:

  Its very painful issue,how u gonna left ur wife and having a sex with a prostitute.A realy man must show a respect to his family.

 13. nazimbiri says:

  MANGANYA CHONDE PALI NKHANITU APA

 14. Yakobo says:

  They should also patrol at a Works Office Garage in Salima. It also has turned to a short time place

 15. kayamawa says:

  Azibambo ndi a Zimayi amene tili mabanja, chonde tiziyesetsa kukwanilisana podya zinthunzi. Ngati sunakhute kumanena ndithu. Ine ndimanena kuti ayi ndithu lero simunandifike tibwelezetso mukapuma (osailwala ka fruit or tea ku bedroom). Mene zakhalilamu Mkazi umaoneka chitsiru/opepela chifukwa anthu amakuona ngati ntchito ya usiku suitha ayi, Amai amene amuna anu agwidwa ku Chez Mtemba, muzisambila mchere daily or kumamamwa tea wa cinnamon ndi (mtentha thupi woopysa umenewu) musanagone mwina abambowa angaone kusintha,
  koma zoseweletsa muli nazo, mukagula mikanda yambiri, ndiponso ndikufunilani bwibwi muzibwila mpaka bamboyu akhazikike. Chonde mukutiyalutsa. Ngati simukutero ndiye ubwino wa banja uli pati, anthu azingoti at ndine Mrs. or Mr……………………………if not alangizi alipo amene angathe kukuphinzitsani kuti anthu okwatiwa muzikhazikika chonde. I hope condom inagwila ntchito yake otherwise matenda tizingopakana.

 16. lonje wa ku poly says:

  thats an indication that God is about to deal with the wicked people soon

 17. Henry Banda says:

  The police officers did well to cought them doing that but why they do not catch those people who kills albinosm Are they receive cash?

 18. issah says:

  That’s good plan people improvement the world change now

 19. Mwama Du says:

  Comment: Pangani zomwezo ndi mbava. KOMA ULOMWENSO SIZINTHU ABALE!!!!!

 20. Mulibwanji? says:

  This is also commonly happening at TNM car park. So long as you have K1000, guards grant you the required freedom. Ma guard akamaweluka, amakhala ndi 40 Pin plus plus,,,,,, this explains how serious chiwelewele is nowadays. Shame on the World. repent and God is ready to forgive and receive you.

 21. Boy b says:

  Mwatani kodi anthuni?

 22. Pitala Mathanyaula says:

  Koma Alomwe anyanay abale, Ku South uko ndiye kuti sachedza ndikuchindana atei? nchifukwa chake amachulukana ngati Mbwewa. What do you think?

 23. Kanundu says:

  Fotseki..mmalo mogwila mbava mukulimbana ndi anthu akudya ndalama zawo..kagwireni ntchito yeniyeni uko

 24. Justice says:

  The POLICE am sure you can do better than just arresting people having sex. Let us have more news of them arresting real criminals who are stealing our property.

 25. cape maclear breacking news says:

  ife timapanga mphepete mwanyanja and muzabwere tizakubizeni madzi

 26. zazii wokwiya wa ku cape maclear says:

  zaziii izi akusowa chochita apolice

 27. Tunthumbwana tambewa says:

  A mwangowachita nkhanza. Galimo yaboma yake? Munangukhumbira mphepo itakung’ambani, moti apolice pa night samumapanga asiyeni anthu ndi ufulu wawo usankha ku room or mgalimoto or kunyumba zonse ndi zawo. Anthu amakwera ndi matenda mu ward kucuipatala, zaziii

 28. hot head says:

  police wat u do shows ur failure

 29. “The car was shaking in a funny way” koma anthu amanyekulilana awa moyikapo mtima kkkkkkk koma alomwe tatchuka

 30. Nankungwi wamkulu says:

  Pano apolice apa Malawi chalowa chiwewe cha Peep show amagalimoto a eni.Some enjoy having sex in the car than in the house.Some get turned in the bush or at the beach.
  Tamagwirani mbava apa.This steamy people are not a threat as longer as they r consenting adults.Mzimayi wokwatiwayi means she was lacking something from her former partner and decided to try another man who could satisfy her.Osamangayang’ana azimayiwa mumanyumbamu ngati azichemwali anu.Ena amafuna ngati dosage ya mankhwalazo.Mmawa,masana madzulo.

 31. Kokotowa says:

  Ine ndimapita ku underground Car park ya National Bank Headquarters! I pay the guards mmene ndaganizira and have sweet uninterrupted sex!

 32. JahFire! says:

  let them fuck¡¡¡

 33. peter says:

  I wish the police would this same level of intuition to pursue real criminals

 34. Aaaaa! Ku chezemtemba? Kumeneko ndiye kochitira mgalimotoko. Kungoti a police amafunanso mahulewo! Sizimenezo ai. Mukulimbana ndi za ziii!

 35. Malipeya says:

  WHILE I AGREE THAT PUBLIC SEX IS NOT ACCEPTABLE, I LAUGH AT THE CHARGE. I THOUGHT WE HAVE PUBLIC NUISANCE AS A CHARGE ????? THIS IS MORE APPLICABLE THAN WHAT POLICE ARE CHARGING.

 36. Michael Saini says:

  Comment Nawonso Adziona Malo Opangila Ma R/house Onsewa

 37. chejali says:

  Kodi ma room akudula mudakayaluka a khakhakha

 38. Michael Saini says:

  Comment Amasuleni Palibe Nkhani Pamepo Sizachilendo Amkapanga Ku Airport Aja Munawatani?

 39. chatonda says:

  Shame on the two especially the married man. Where is his respect now? The damage this issue has caused to the two is too big to be filled regardless of how long this issue will take. It will be with them until death. Sorry for being known the shameful act- sex in a public place.

  Now police officers are not aware of the correct Charge for such offence. It should be conduct likely to cause indecency or violation of public decency in Law. The brutal Police officers should know the constitution of Malawi better before they take suspects to court.

 40. short wamtali says:

  Mukuonjeza fans…….ena ndi awa akulowa pa car park ya TNM. Ma Gurd a G4S anapezapo mgodi wawo pamenepo amalowetsa magalimoto fans ikathana imasiya kanganyase pa gate.

 41. MUSSAM says:

  MWASOWA ZOCHITA APOLICE

 42. Mwinifilimu says:

  kudya nkudya

 43. Pali nkhani pamenepa? Malamulo enawa are very colonial & archaic. Uku ndi kupatsa ulesi apolisi. Instead of focusing on real issues they are busy catching ppo who r enjoying themselves in the comfort of their cars.

 44. big man wamkulu says:

  thyolo, mulanje, cbiradzulu, blantyre…..

 45. mathola says:

  zopusa why not to deal with thieves just leave them they were injoying

 46. denga says:

  zopusa

 47. Ambulaje Ambulaje says:

  Accommodation charges alternatives!!!!

 48. chindi says:

  apolice mwasowa chochita gwirani mbava tikuti mbavaaaaaaa

 49. Chilmoni tweet says:

  Palibe nkhani apa ndani satero khaya nyumba pathengo munjale

 50. PANALINSO ZA CHISHANGO YAPA ??

  MWATENGA MATENDA KAPENA MIMBATU APA !!

 51. Sylvester says:

  Inu apolice!

 52. Kumafinals kwa dziko uku but its better than gay or ……..

 53. hidgeman masina says:

  Comment KODI APOLICE MUNASIYA KUGWIRA MBAVA NDIKUYAMBA KUGWIRA OPANGA CHIGOLOLO? NTCHITO YANU NDIKUGWIRA MBAVA OSATI ACHIGOLOLO NTCHITO YANU YAKUKANIKANI, NDINU MBUZI MAPOLICE NONSE.

 54. edda mwalweni says:

  I hope girls are now cheap in bt mpaka kuchindira mgalimoto lo!!!!!!!!!!!!
  You are missing the sweetest part of it by doing it in a car.Plz try to find better places for doing that not in the car.We are God’s image.

 55. N.zinyongo. lilongwe says:

  The last days

 56. ENOCK ALIMOYO says:

  CommentDONT GET SURPRISED. THESE ARE SIGNS OF THE TIMES

 57. kangaude says:

  Kodi apolisinu simumanyenga? Mmalo momagwira mbava kumalimbana ndi opanga zigololo zoona? Kupusa eti!

 58. odzisata says:

  Tawauzani ma bwana akumasinjila mmagalim oto mma carpark kuti mitengo ya ku ma lodge kuno ku Blantyre ndi iyi: Chikunda coach house (bangwe): kucheza K5,000, kugona K10,000, Khuluvi motel (chatha in chileka): kucheza K3,500, kugona K7,000, ku ma China (chatha in Chileka) kucheza K2,000, kugona K8,000, Big Brother (BT CBD) kucheza K2,000, kugona K8,000, Caesars palace (BT CBD) kucheza K2,000, kugona K8,000, Tikwiza (kameza) kucheza K1,000, kugona K3,000, Kutsalankuti resthouse (kameza and Lunzu) kucheza K5,000, kugona K10,000, vicky motel (lunzu) kucheza K5,000, kugona K10,000, Nkhulozwe fiti zagonja (lunzu) kucheza K2,000, kugona K5,000, malayina (magalasi) kucheza K5,000, kugona K10,000, Paseli Lodge (ndirande and Lunzu) kucheza K5,000, kugona K10,000, XL lodge(greencorner) kucheza K5,000, kugona K10,000, Ku malekano resthouse (ci): kucheza K700 kugona 1000, kwa mbwelera kucheza K650 kugona K1000, Zikomo resthouse (mbayani): kucheza k1200 kugona k3500, wayede resthouse: ‘ucheza k350 kugona K700. Mkango lodge: salola shorttime, mungo lodge salora shortime, superior Hotel saloranso. Ndikafufuza kwina ndikuuzani zikomo

 59. Dr.Jack says:

  NO SECRET IN THE DARKNESS, LIGHT SHALL SHINE UPON IT. WHAT A SHAME ! AMENEWO AKWATILANE BASI KUTI ZAO ZIWAYENDERE.

 60. JACOBS says:

  Comment ALOMWE!!!!!!!!!!!!!! WOYEEEEEEEEEE!!!!!!!!!!!!!

 61. Iyeyo says:

  What is wrong with them having sex in a car, its not like they are doing it outside for every one’s view, they are doing it in their private space, inside a car…i honestly find nothing wrong

 62. Mwakipiki says:

  Police, how can you say these people were idle and disorderly when they were busy shaking in the vehicle? They were so orderly by taking it privately into their car. What you police have done is invasion of these people’s privacy and you need to be sued!

 63. Okhrana says:

  Mukungoti alomwe alomwe, chani? Mukunenanu tazamlaweni mkadzi wa chilomwe, uzizafuna utachita even akusamba kukoma udyo anthufe(alomwe-fe) za edzi dnt ware highest population is mangochi kwa ayao and karonga kwa atumbuka

 64. collins says:

  Comment;not ok

 65. A Chivunde Kodi Alipo? says:

  Mtundu walomwe ndiumene ukubwezeretsa chitukuko cha dziko lathu mbuyo. Chikanakhala chimanga, tikanachisokera mmasaka limodzi ndi anankafumbwe kuti chonse chivunde, nkukachikwirira kwao ku mpulo wa bata.

 66. Sungununu says:

  No story apa, atayeni basi. Nsanje bwanji apolisi.

 67. mordecaizgambo says:

  dats is furish anthuwo anali malo obisikatu chimene inu mumawamangira ndichani.phuma ndi nyere tu sizimalinkana maguys

 68. okhudzidwa says:

  Sinkhani iyi…malawi wise up* apolice moti azilimbana ndi mbava.apa*

 69. Rodriguas Latata says:

  Apolisi musamale keneko mugwira mkulu wa a Lhomwetu. Eeh! Eeh!

 70. Bolingo wa chingoni says:

  Alomwe kukonda kudya gondolosi muyamba kunyengana poyela ngati nkhuku.

 71. chikoya says:

  kodi mgalimotomo amachita disorder kwa ndani? apolisi, imeneyo ndi tresspassing into someone’s privacy.

 72. gondwe says:

  I will be their defense lawyer. POLICE BRING EVIDENCE. basi akagwa nalo funso limeneli. and was-out case

 73. zoona says:

  nothing worth making a news headline here…..ndi angati amene sanachitepo izi pa paris, bwandiro,africana,club G string….makamaka pa idols? Kkkkk komabe penapake mpakana kuvula zonse in a car quickie?

 74. Jihadi John says:

  I have never seen a worthless institution like the police service. Kutereku sanawaninke Ja 2pin basi ali public disorder. Given a chance, I can behead all these police sluts! They stink!!

 75. mbani says:

  Alomwe muvuta ok NAC was formed coz of Alomwe eeti

 76. frank says:

  Alhomwe mwachukatu ndi nkhani zanyatsi, munakhala bwanji inu alhomwe.

 77. Nankungwi says:

  umve!

 78. Andy moses says:

  Last days soldom and gomorra.

 79. Zikundu says:

  Hey! Police, those people were not idle, and to who did they bring disorder? Get life guys. Be serious too.

 80. mr chimbwititi says:

  gwirani mbava osati ochindanawa.a PSI anawapasa makondomu kuti azichindananilana ndiye mumange a PSI basi.

 81. Cadaver says:

  How can it be IDLE when the car was shaking? wrong crime…idle and disorderly? kkkkkk
  the two were not idle, they were busy to the extent of the car shaking!

 82. Kankobo says:

  Ine ndimachindila mchimanga..apolice sangandipeze

 83. MELINDA says:

  THESE CHEAPER MEN DOES NOT KNOW HOW TO USE CONDOMS.

 84. Mr.Phiri says:

  Tabweran muzagule malo akulu kuno ku zomba 0888650333

 85. nyani ndi munthu says:

  kumkwatana ndi kokoma,nde mukumatigwira chifukwa chani!

 86. Zipatso za satana, tili munthawi yotsilza.

 87. Dan says:

  Zachamba

 88. pido says:

  koma nde ziliko

 89. jn says:

  So the police went to a car park at a night club for a patrol?

 90. Ashraf Kumar says:

  Za ziiii..akutikhapa mmakomomu and all you can do is go around looking for ‘funny shaking’ vehicles!!!

 91. mwiithotho says:

  Amangenii

 92. Caesar m'bama says:

  Eeeeeeeeeeeeee ndiye akamva Alamu kunyumba pavutatu apa kkkkk

 93. Dambo says:

  kkkkkkkkkk apolice naonso amangidwe coz nzawo amulepheletsa ntchito ili mkati akumva kukoma

 94. Wakukaya says:

  Guys nanga clip yilikuti kut tiziwe kuti amapa sex. We cant use the shaking of car as evidence that people are doing sex?. This is a fallacy because shaking of the car and doing sex are two dissimilar things. This is not true. May be there was wind that is why the car was shaking.

 95. chris says:

  Its safe, not so bad

 96. puludzu says:

  Blantyre sidzatheka pankhani zotelezi. Kuno ku capital nyasi zotelezi kulibe koma alomwe ukonda masewela otosana mmimba mtundu uwu sudzathekanso ayi. Izi nizipatso za mlakho wa alomwe. Nanga anthu oika mabele pamtunda mmati atani ndi khalidwe lawo basi losadzisungila ulemu. Kwakhala ngati Agalu.

 97. fisi matama says:

  Alakwa chani,a police mmalo moti mudzigwila mbava mukalimbane ndi izii? Nyapanu!

 98. Tapa says:

  blood ikayamba kugogoma munthu sungachitile mwina…moreover anthuwa samapangila pabwalo anali mgalimoto….so to hell wit d police..moti azigwira mbava …mxiiiiiii

 99. Tapa says:

  mtima ukakankha mwazi munthu sungachitire mwina…

 100. jojo says:

  sex in car is so sweet…..what’s wrong anali panja ngati anazikhomelatu which was Private …kusowa zochitabasi. nanga sex in cell.

 101. baliman says:

  Kusowa zomangrana eti, munatan osangopempha kut nanu mulaweko? Jerous basi, uchindere!

 102. william malabo says:

  Apolisi kusowa ntchito mmangodya ndalama za boma zausilu

 103. mwamusanga says:

  End of the World, wake up and pray!

 104. crispen kandido says:

  police are failing to most of the real criminals (e.g. thieves) but are just disturbing soft targets of people who are enjoying their lives. shame

 105. Nkhani yopanda pake ngati iyi nde paliponse newspaper,tv,media,koma zasowa ndalama ku capital hill no report mwanyotsolana nokha-nokha agalu,asatana inu.4tseki!!!!!!!!!!!!!!!!!!

 106. Tengupenya says:

  Kodi kunalibe mdima? Mwini wake galimoto anadandaula? Eni ake car park anadandaula? The space inside a private car is private space, even when the car is on the grounds of a public car parking area or anywhere at all. The two are adults who were expressing affection to each other in the privacy of their car under the cover of the darkness. To see them one had to draw the curtain. Ar we becoming a moralist society with morals policing in dark car parks? Once the police ascertained there was no harm against property or life, they had no further business with the car or its occupants.

 107. xxxxxxxzzzzz says:

  Osamalemba zokhuzana ndi atumbuka ali pheee…….sitingatukuke nazo izi….lets have positive minds please….poti ukamalimbana ndi mtundu kapena munthu, iyeyo amakhala akupita chitsogolo iwe ulibe pomwepo….lets think positive guys.

 108. chilungamochiwonwke says:

  ntchito yabwino apolisi koma nanga umbandawu ukukukanikani pati? tathanani ndizikuluzikuluzi kaye kenenako kumalizila zochepazi

 109. ndaona says:

  A police ntchito mukugwila koma nanga a cash gate mukuleka kuwamanga bwanji. Mukulimbana ndi chilengedwe bwanji, tawagendanitu miyala ngati inu muli clean

 110. ndafakale says:

  Apolice asowa wogwira.mbava zavuta bwanji mulimbana ndi zachabe.

 111. Doctor says:

  Hey Guys!!! Bwanji Kodi??? Mudzipita ku Big Brother close to TNM offices. Very secure and private. Ife timapita kumeneko kana samatigwira. Agalu inu.

 112. Mbola says:

  we are fed up with your foolish comments attacking the Lomwe. Each and every petty issues done by the Lhomwe u take advantage over them to castigate. That’s the sign of being afraid of them. Mind u, Southern Region will remain in power while the northern region will remain CSO leaders until Jesus comes.

 113. common sense says:

  Get better articles. Not shit

 114. misheck ogar says:

  Njala siimaona malo ikawawaComment

 115. Milankho yoka yoka chisembwere nde chawo they are still using Condoms donated by NAC

 116. D says:

  Koma pena pake Malawi Police Services your priorities are upside down. People are literally staying awake the whole night trying to protect their houses, and others are hacked right in front of their families – inu busy ndi zimenezi? Shame on you!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!

 117. bentby smart says:

  Dzikoli lili mmanja mwa Agalu(devil)

 118. Francis says:

  Galimoto ndi yandani, vuto lanu ndichani? Pangani zanu

 119. ... says:

  It is at your own risk moving 200 meters around Chez Mtemba. That is hot entertainment place. Just go through newspapers and see pictures for how people entertain themselves at Chez Mtemba. Arresting these people over entertainment its just breaking their rights. Imagine around 10 PM. This is time for the Lomwes to enjoy. Leave us. Money its a problem if there is any problem then its how to spend it.

  I know for sure these policemen are Tumbukas. ATumbuka mugwa nayo game, for 5 years mukukongotisatira ife a Lomwe ndi kochindana komwe. Timothy Mtambo akutisata ma action onse tikuchita, tangoonani nacgate. Lero maconstable a chitumbuka agwirizana kuti azitisatira ku ma enterainment komwe. Nophiya woyee.

 120. nayongo says:

  Koma chiwewe chake abale please aaaaaa. Ndiye mwati edzi itha? what is worng with people olo nyere zakeko ndiye zaukalitu

 121. Machende A mbuzi says:

  Aaaaaargh. A police a pa Malawi mwayamba za utsiru. Bwanji osangolandira ka mmanja and let them fuck in peace. Mmalo moti muzikagwira akuba you’re wasting time persecuting and prosecuting people who just wanna have fun

 122. wanyabuvi kate says:

  ALOMWE ALOMWEEEEEEEEEEEE! NOPWIYAAAAAAAAAAAAAAAAAAAAAAAAAAA! KAPENA KUPWISAAAAAAAAAAAAAAAAAAAAAAAAAAAAAAAA! KAPENA ZOPUSAAAAAAAAAAAAAAAA!

 123. unzwede says:

  Uncontrollable nyere. Anthu kupenga nazo, nchifukwa chake akungokhwethemulirana paliponse. MUKANGODULITSA NJOMBOLOZO zingakuyalusiseni.

 124. Chatty Man says:

  Fast and furious!

 125. Achimidzimidzi says:

  ZANU zimenezo inu Ahlomwe. Kupanda ulemu basi.

 126. eric chidiso says:

  where is malawi driving to? Having more hiding places very shame.

 127. mbambande says:

  Sopano mwaziwa chifukwa chake Mangulama ndi Siyani, Mulli, Thodi ndi Jana, Mpulula, Mwanamveka, Mathanga, ndi anzawo anakatenga ndalama za NAC kugula ma condom. Alomwe kukonda chigololo too much. Aliyense ndi wache mu Mulhakhomo. They are Mulhakho couples…

 128. chaiwone wawo says:

  Why was this second couple arrested? Its in the night and at a night club. Its not at a hospital premise. This second couple is not wrong. there were at a place where such acts are a characteristic. Unless am told that having sex in a car is a crime, which i don’t believe is the case. Usiku ku night club. Kunalibe ana oti atha kulaulidwa. Anthu opezeka kumeneko ndi akuluakulu okhawokha woti amapita either for beer or mahule. alakwa chani awa?

 129. Francismagowa says:

  Koma Game Mbola Kulibe Kukoketsa Night Akugwila.Komano Mlandu Waku Court Azikati Chani?~zili Zonse Ku Court Anthu Akuupeza Mgalimoti Mlandu Nawoni.Aaaaaa Zili Ku Nyasaland Macheza Achoka Nyumba Kufika Mgalimoto.What A Game!!!>kapena Ndima Way Game A CAF Al-Hilal 4-0 Bullets.Kikikkkkkkk

 130. nazimbiri says:

  azibambo aku BT kumwa kwambiri mtototo.sagona usiku uli onse upeza anyamula chikheba,akuuza londa kuti ukangouza amzako,iwe ndikuchotsa ncthito.hahahaha

  Kodi satana ankukhalirani pa msana?

 131. herman shaba says:

  Zopsa… Moti mzilimbana okuba avutawa…akutibera magalimotowa…bax buzy ndi anthu oti sakuba…sakupha..kom akungozipepexa…mmmxxi

 132. Comment police should make more sport check @ different drinking place in the conutry and this is real,and sex is happening in our bars.

 133. vyamuvisulo nthengwa says:

  alomwe mwationjenza muzinyenga nokha kodi magondolosi mmadyesana aja ameneo

 134. Mercy McLean says:

  Asiyeni anthu adye ka quickie…. ask us ! kkkkkkk

 135. taelo limmbani says:

  sorry kodi chikuchitika ndi chiani. Aids singaathe kuno ku malawi. Chifukwa azibambo achilomwe kudya gondolosi ngati nsima

 136. Mkango says:

  Nyasi

 137. nazimbiri says:

  Omwe amakonda kwambiri chigololo masiku ano,ndi akachilombo.amafuna kuti apite ambiri.Chonde titothatu ndi matenda kunjaku kwaoopya.paja masiku ano gondolosi, mvunguti,mkwapukwapu amapezeka ndi aliyense.

  Chonde apolice tithandizeni kuthana ndi anthu achisikawa.

 138. mona says:

  Alomwe Alomwe

 139. Kalembeni Kathawe says:

  Tawauzani ma bwana akumasinjila mmagalimoto mma carpark kuti mitengo ya ku ma lodge kuno ku Blantyre ndi iyi: Chikunda coach house (bangwe): kucheza K5,000, kugona K10,000, Khuluvi motel (chatha in chileka): kucheza K3,500, kugona K7,000, ku ma China (chatha in Chileka) kucheza K2,000, kugona K8,000, Big Brother (BT CBD) kucheza K2,000, kugona K8,000, Caesars palace (BT CBD) kucheza K2,000, kugona K8,000, Tikwiza (kameza) kucheza K1,000, kugona K3,000, Kutsalankuti resthouse (kameza and Lunzu) kucheza K5,000, kugona K10,000, vicky motel (lunzu) kucheza K5,000, kugona K10,000, Nkhulozwe fiti zagonja (lunzu) kucheza K2,000, kugona K5,000, malayina (magalasi) kucheza K5,000, kugona K10,000, Paseli Lodge (ndirande and Lunzu) kucheza K5,000, kugona K10,000, XL lodge(greencorner) kucheza K5,000, kugona K10,000, Ku malekano resthouse (ci): kucheza K700 kugona 1000, kwa mbwelera kucheza K650 kugona K1000, Zikomo resthouse (mbayani): kucheza k1200 kugona k3500, wayede resthouse: ‘ucheza k350 kugona K700. Mkango lodge: salola shorttime, mungo lodge salora shortime, superior Hotel saloranso. Ndikafufuza kwina ndikuuzani zikomo

  1. Nkhedu says:

   Man koma ndiye mumazitsatu?

  2. wodabwa says:

   umayitha ayise mpakana ma 350

 140. Tsikulokufanyani says:

  Koma ku Blantyre chigololo chabebatu!!!!!!!!!!!!!!!!!!!Akazi mmanyumba chenjerani

 141. afana says:

  Kodi ndi ndani samachita sex? Kukhala ngati zodabwisa bwanji anthu akamapnga zimenezi? Kupanga ndikupanga basi,,, ngati simunyenga ndiye muziwayalusa anzanu? Muli shupita

 142. Matokoso says:

  Big up a polisi for checking up on this shaking in a funny way motikala. Amakhala munthu atamusekera ku buti

 143. kanyika dk says:

  eeeh alomwe again shaaa.dziko liri manja mwa big dogs

 144. Should we call this a car sexgate?

 145. FANNY ———LAZY DAYS.

 146. kachindam'bwete says:

  Zanyanya man, zimenenzi mseteComment

 147. Kodi anthu aku mwera mwayamba chisika, ngati agalu eti? Dziko la malawi lapepetulidwa ndithu.

 148. wautali says:

  Comment moto moto moto mkalaya

 149. Tili kwa eni says:

  Akuba onse ati mbweewa kuti muwagwire mukulemphera koma opanga chigololo ku chez kapena vakabu yomagwira anthu omwe acheledwa pa maulendo awo. Gwirani mbava osati zimenezi. Anzanu amagiligishana ndiye inu zimakupwetekani poganizila kuti muli pamphepo.

 150. Lazalo says:

  A good topic for research.

 151. eye witness says:

  mulomwe winansotu uyu!!!!! your godfather is painting walls and you are busy painting Vaginas eeeeh!!!!

 152. Rhodriguez says:

  Kwinaku akumvera NEPMAN “Na lero” kkkkkkkkkkkkkkkk

 153. koma mchiyani amalawi kuyaluka chotele!

 154. Manyasa says:

  Alomwe kikikiki

 155. davie says:

  hahahahaha

 156. Mercy Thindwa says:

  U said married man and prostitute…. is a married man not a prostitute??? why he left his wife for another woman.

 157. nyenga man! says:

  Apolisi tagwilani mbava zeni zeni, nanga inu simumanyenga??

 158. manyi says:

  Nkhani zakthela eti iwe sumachita chigololo?

 159. matako m'mwamba says:

  Asiyeni amenewo amamvana kukoma kkkkk. Chigololo cha m’galimoto kuuuukoooomaaaaaaaaaaaaa! Apolicenu ndinu mahule oopsa kuposa mwawagwirawo.

 160. Zolaula basi.mwatani aMalawi?

 161. Nasirina says:

  Komwe titafikire June! Gule aliko.

 162. Mwena Malawi Origin says:

  Kuphedwa kwa ma Albino,, kugonana kwa mumagalimoto , Akuba mpaka kukalowa ku nyumba ya veep ndi za nduna , kupenta cell zonsezi mu Boma la DPP kuzera ku utsogoleri wa APM.

 163. Tidzingonyengana ngati nkhuku chonchi?Nyumba zimadula kapena chani?Bwanji simmangopangira pa tchire?Anthu ocititsa manyazi!

 164. wanda says:

  Inu Apolisi mumagonana nokhanokha mukamachita patrol, ndani amakuzengani mlandu. Nsanje ndiyo yakula apa. Mumafuna kuti mukagwila mahule inuyo muzichinda, enawo ndiye kuwagwira. Muzayese dala kugwila ine, mdzakufailani doom. Stupid police. Zaziiiiiiiii!

 165. bamitutu wings. says:

  All this people the’re under age, they can not allow them to go to the resthouse or hotels. so leave them to do there jingo janga in the public hahahaha !!!! funny malawi.

 166. Special advisor says:

  Sex is happening everyday, everywhere – under a tree shade, in the bush, in cars, in offices, in public bathrooms, on buses, etc. What is our collective morality on this? The offense/charge should relate to what we have collectively agreed to be a ‘normal, acceptable way of living”, and this should be in our laws. “Idle and disorderly” is an idle charge. It is petty and frivolous. The norm is for every social ill, is to issue public warning and education. We can’t have naughty police personnel that selectively launch a campaign on ills, merely to cause embarassment to people that are out having fun. Yet they look away from, and are sometimes part of, the real serious rot in our society.

 167. fkr says:

  why not go look for real criminals?

 168. lol says:

  Koma B. Town tamakamba nawoni, amangofuna kenakake or ka hands

 169. weniweni says:

  Koma dziko iliiiii thats bushit

 170. Ndadya Zanga says:

  That was at night 10pm. Why catching them. That was discipline enough to enjoy at that late hour in the car. You made a mistake disturbing them. I hope by the time you came to disturb, they were already done with the enjoyment. Tikufuna muzigwira mbava osati amenewa ayi.

 171. mulkho says:

  koma yayaya atindichani kwenikweni

 172. aishoshe says:

  koma anthu aku Blantyre mwafatsa..kapena kwagwa mulili wa nyere?.

 173. Yonas says:

  Come on, zero in on criminals and not MERRY MAKERS at owners behest love birds, POLICE PLEASE !!!!!!!

 174. Maunde says:

  Point of order. Why is it you a married man and a prostitute? It is out of order to say a married man but you say “a womaniser” that’s better

 175. Kulibe ma room ku malawi eti? Bwanji ayamba kugonanirana mumagalimoto? Shame to them.

 176. Patriot says:

  Kikikiki Anthu akunjoya kugawana Aids inu mukuti ayi.
  Malo mokamanga apolisi anzanu akupha anthu osalakwa ku Lunzu.

 177. bakayawo says:

  Koma a polisi muli pa vuto lalikulu. Ndi manyumba angati anabedwa pa tsiku limeneli koma okuba osagwida? Mukulimbana nfi anthu amene amanvana kukoma? Shit! Uku sikuchipatalatu uku. Muyambenso patrol kutchire koz mmatengomu mupeza ambiri

 178. Kuteloku ndigonana mgalimoto ndi mlandu eti?Koma Abale kupanda galimotokunso penapake sibwino bwenzi malamulowa titawadziwa kale.Nanga galimoto lili lako ungakhale pa mlandunso?

 179. otate says:

  A police mwasiya kugwira akuba usiku muzigwira zimenezi?beautify Malawi kodi?

 180. aquar says:

  Commentasaaah

 181. Angofuna kutchuka panyasa times ndikaonetse palibe nkhani yogwira mutu koma amene agwidwa lelowa ndie lalibe ndingayankhule chifukwa angofana agalu okha okha olo mmene ikuonekela miyendo ya mkaziyo abambo adamuona bwino chifukwa udali usiku koma masana akadiima mutu kuti palibe chovekela ndi mbiri ndi nkazi ameneyo ai bola adathetselapo ludzu la zopusa zakezo koma magalimoto akunakhala awo anjonda zimenezi eti

 182. jeaytee says:

  Its tym no wonder.

 183. zaya says:

  Another Lomwe caught in the Act.

 184. Ndasiya kukoka mahule

  1. kalasa kondwani says:

   last days

  2. Hahahahahahahahahahaha milandu ya cashgate mukukanika zaziiiii

 185. Ineyo says:

  I thought the indecent behaviour offense has to do with both time and place? How does a funny moving car near a pub at night become police business?

 186. midnight 6 says:

  Alomwe enanso awa, Osakapangila ku Thyolo bwanji?

 187. midnight 6 says:

  Alomwe ena amenewa, osakapangila ku Thyolo bwanji?

 188. Rafik says:

  koma alomwe mwavutatu

 189. amakhosi mukulugenzi says:

  Mmmmmmmm kwavutatu

 190. tuvi says:

  koma alomwe,alomwe, ndi chiani? kuba,nokha, uhule nokha kuzikonda nokha you need deliverance

 191. mlomwe says:

  Alomwe ayayayayayayayayaya

 192. Ujeni says:

  Comment zamanyazi

 193. thoko says:

  Kkkkkkkjkkkkkkk apolisi kusowa zochitaaa chani?

 194. hendrina says:

  hedee!! uluuuu!!! wadyera katundu mu motikala. kodi ma resthouse kunalibe???

 195. mbwaxe says:

  Kudya kwa alomwe ndi chigololo!!!!!! Wina ndi mulomwe wa sda ku area 14 ku lilongwe!!! Kunyenga too much!!! Kubaso tooo much!!! Akumanga ti ma den akuba ndalama za church!!!!!!

 196. kapy says:

  nkhanizi zikuchuluka bwanji?

 197. master says:

  PLIZ arrest lutepo, kasambala, peter mutharika of 92 billion, JB they have stolen our billions, why waste your time arresting people for doing sex??????? u r failing to arrest mafias who have stolen our billions, arrest MULLI for failing to repay 3 billion loan to MSB this country wil nvere develop ndithu!!!!!!!!!!!!!!!!!!!

 198. Charles says:

  Pali nkhani apa mwasowa zogwira eti osapita kumakagwira zigawenga uko bwanji zopusa basi

 199. Paul Vida says:

  Zopanda ntchito zimenezo mukulephera kugwira anthu akuba omwe avuta ma locations basi busy busy kulimbana ndi achiwelewele. Fuck off!Comment

 200. A Human Rights Akuti Chani Abt Dat Isue?

 201. mboma says:

  Alomwe asogolatu apa, mitundu yinayu mukutani?? akuposeni zonse zoona???i now understand why they r overpopulated and end up begging in streets!!!

 202. ManVince says:

  Akuba akukukanikani kuwagwira koma anthu amenewa nde mukuwagwira mwakathithi lol… Our police

 203. Jackson mzoza says:

  shem kufuna kufuna kutchuka

 204. Zantchito says:

  Koma abale ku BT kwavuta. Zoti ena agwidwa tsiku lomwelo sanamve? Komanso mphongozo ndi za ku Lhomwe Belt kokhakokha. Mukudya gondolosi kapena mthibulo alhomwe inu?

Comments are closed.