Email a copy of 'Anti-child marriage campaign launches in Ntcheu' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Anti-child marriage campaign launches in Ntcheu' to a friend
Following the positive response the movie B`ella has received internationally, its director, Tawonga Nkhonjera has decided to form Nyasa Films...
Anawa anyanya matako kukula kuchita kuposa makolo Mwina ndizakudya tikudya masiku anozi. Anawa anyanya mbina, Akamati ndi wa 15 years ngati wa 23 years. Ndiye sitivalanso bwino ntchafu pamtunda
Adzidukula pamaso pa azibambo?
Chonde amfumu anuwo aleke kunyenga anafe
KU BALAKA KUNONSO MUBWELE !!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!
Koma azimayi apolisiwo kutupikana kumeneko anganthamangitse wakuba. Not surprised crime is sky rocketing in Malawi.
Kukhala chitsanzo chabwino sikugwila tchito yapamwamba kokha, koma kudya mwanzeru ndikofunikanso, kutupikana kumatako chepetsani……………
Kodi azimayi vuto lawo ndichani zilizonse adukulepo basi, pali chifukwa chomveka choti avinevineponso apa?
Ndichitsanzo chanji mukupereka kwa mwana wamkazi, azidukula pamaso pa azibambo?
ikalawa zamchere simva tiwonera inu tiyeninazo
Walemba nkhaniyi. Mahwayo mkatimo mulinso mahwayo muli pheeeeeee