Email a copy of 'APM campaigns for his 'replacement' in Thyolo East' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

13 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
godobaman
godobaman
9 years ago

baby iwe ndiye uiti wabwera liti dziko lino ukulidziwa komwe linachokera iwe samala ndimalankhulidwe ako ngati ndiwe mulomwe dzako izo

zotsatira banda
zotsatira banda
9 years ago

mbava za DPP convoy mpaka galimoto 40 koma yaaaa kuwononga dola zathu za misonkhoooo

The Country Chief
9 years ago

Zazii,wa opposition nde angamanidwe chitukuko,kusankha munthu ophunzira sikwabwino et,mesa wa opposition yo amakhala kut ali m’boma kale,cjimasiyana ndi chan,anthu aku Thyolo pliz sankhan wa independent kumeneko asachite kukupangiran zochita,chisankho chili mu mtima mwanu

DR. SAN- ABACHA . WAKUMALOWA -KWAMAGODI
DR. SAN- ABACHA . WAKUMALOWA -KWAMAGODI
9 years ago

Koma ashado akewa malaya akuchita kukhulumba, mutuwo ngati chikula mayembe koma kupaliament ko akayankhulako , kamwayo ngati afuna aziti,moseliwa khanyenekikikikiki.

Kwima
Kwima
9 years ago

Kkkkkkkkkkkkkk!! Ku nyasa patala plasdent walomw koma kuli anthu owoneka bwino kumeneku ku tyoloku

ndangodutsa chisale
ndangodutsa chisale
9 years ago

MUST was shifted to Thyolo by your arrogant brother. There is nothing you did for that constituency save for what your brother did.

baby
baby
9 years ago

Koma ndiye APM anthu ena mumadana nayetu.

Zondiwe
Zondiwe
9 years ago

Yesterday, I saw the President’s convoy coming from campaigning in Thyolo and it was one of the longest Presidential convoys I have ever seen. It was probably 1.5 to 2.0 kilometres long. Much longer than any of Jb’s convoys. Literally hundreds of vehicles.
They say the more things change, the more they remain the same.
It appears once power is tasted, all values are thrown out of the window!

Kanyani
Kanyani
9 years ago
Reply to  Zondiwe

Convoy ya president imathera pa galimoto ya polisi imene imakhala pambuyo. Enawo amakhala ongolowerera kuti ayende nawo mwachangu. President Arthur Peter Mutharika amayenda ndi magalimoto khumi basi.

Yobe boo
Yobe boo
9 years ago
Reply to  Kanyani

Kanyani ndiwe waboza, ine ndinalikonko, anali ndimagalimoto ochuluka zedi, kuposa 20.
Musatinamize apa ngati mumadya limodzi ndikutionongera misonhko yathu.

Kulira
9 years ago

This guy is so tacky are those notes in his right hand?????

John
John
9 years ago

Yes DA that is what he is saying. Oh and he is also hitting the point home that, if you are not an MP of DPP, the gvt wont help you develop your area( or hear your peoples concerns) no matter how ligitimate they are. And we wonder why the NORTH is taking matters into their own hands and why there is the “us and them” syndrome in Malawi. Thats is straight from the head of state!!

Read previous post:
Archbishop Msusa clarifies on naughty cleric’s funeral ceremony: ‘He received sacrament of penance’

Archbishop Thomas Msusa of Blantyre Archdiocese has clarified on why the late Fr. Danasiano Kunkeyani was buried at Limbe cathedral...

Close