Email a copy of 'Asu can be released: Wanderers coach fed up with Cameronian striker' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Asu can be released: Wanderers coach fed up with Cameronian striker' to a friend
Malawi Police managed to arrest a gang of suspected robbers who shot dead a police officer who was in a...
kamfana its ASU God bless u. i think u are well educated on issues like this .the staffs themselves cant tolerate that at thier various jobsites but when it comes to football it becomes a taboo.my talent speaks louder cuz of hardwork and GOD .thanks to all my fans love u guys
Matama ma Noma.Athu a local ali momuno ndichiyani chokatengela player ku Cameroon pamene mulibe kali konse?
Giv his money pliz,,,,,remember promise z credit,,,,,ngat vep yakukulira kananji pliz u can jus step out not kulankhura zopanda nzeru
Kkkkkkkk
Matama ngat muli nd ndalama,mulipilen munthu zitsilu inu
Ikanakhala nthawi yathu tikanamusayina Asu
Atsu ndi player wabwino koma akulakwa kusamvesa zomwe akufuna awonderes ndie its okay apite or apeze team ina muno ngati itakwanise zomwe akufuna iyeyo
KODI FAM IKUTIPO BWANJI APA?IKUNGOWONELERA MAVUTO MPAKA AFIKE POIPA?KODI IWOWO A FAM NGATI MANTHU WA MPIRA,SANGALANGIZEPO APA?OR ATANGOMVA KUDZERA MU ZA M’MALUWA{WITHOUT OFFICIAL REPORT}KUFUNSA PLAYER NDI KOCHIYO PLUS EXECUTIVE.MUNTHU MWAKAMUTENGA KWAWO,KUMPLOMISA NDALAMA,KENAKA KUKANIKA KUMULIPIRA NDIKUMUUZA KUTI ACHOKE,PALI NZERU KOMA?OR UMUNTHU ULIPO APA? THINK IT VICE-VERSER IF U WERE UKANANJI IN CAMEROUN}.MUNTHU SANAKHALITSE,MWADANA NAYE KALE BABA MWATANI?ZIPATSENI ULEMU.NTCHITO IMATHA ANTHU NTHAWI ZINA CHIFUKWA CHA KUZIKONDA NGATI KUMENEKU.NA ASU AKACHOKA PA CHIFUKWA CHAKE CHOMWECHI,TSOKA WINA LIMTSATIRA.CHIFUKWA MAJORITY SINATSANGALALE NAZO.KODI PRINCE JERE UKUTI BWANJI?KAPENA MWATAFUNIRA LIMODZI NDALAMA ZA MWANAYO NDI KANANJI?NKHWIDZI NDI KUZIKONDA KUMENEKU KUTHE PULIZ ABALE.POMWE MUNKAPANGAN NAYE SIMUMADZIWA KUTI MUZALEPHERA KUMPATSA… Read more »
NO NO NOOOOOO!!!!! Kananji this is NOT the way we go.Asu is ABIDING BY HIS PROMISE U GAVE HIM.BY 31ST MAY U WERE SUPPOSED TO PAY OUT ALL HIS ARREARS.IF U BOOT HIM OUT,IT WILL MEAN ILL TREATMENT OF PLAYERS.EVEN IF SOME OF HIS FRIENDS FOLLOWED SUIT,IT IS UNDERSTANDABLE.DO U HAVE UR POLICY DOCUMENT?WHAT DOES IT SAY ON THAT? THE MAN IS HAVING HIS FAMILY/RELATIVES,SO HE WANTS HIS MONEY AS PER AGREEMENT.SHAME ON U KANANJI/KODI OR ATAKHALA MWANA,MWAMULONJEZA,NTHAWI IJA YADUTSA,SONO MWANA UJA AKUKANA CHAKUDYA,NDIYE AMATI CHOKA PA KHOMO PANGA?AYIIII!INDE MULI NDI MPHAMVU A COACH,KOMA EXECUTIVE IS ABOVE U.WHAT DOES EXECUTIVE… Read more »
Kudalila company yoongola mangalimoto kujapan kikikikiki mupatseni ndalama zake Asu musamubele ayi . Mukufuna achita kubweletsa bokohalamu kuti mumupatse ndalama makape anoma