Email a copy of 'Balaka police recovers two dead body from a river' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Balaka police recovers two dead body from a river' to a friend
Malawi President, Peter Mutharika, will Friday January 16 visit areas hit by the recent heavy flooding and people affected by the disaster...
Makani sakuthandizani mungokhalira Kutukwana athu ,amenewo asamukile kumitunda asadikile kuti chachikulu chichitike
very sad
MTSRIP. Interesting writing from the writer.
basic English – One “Body”; Two “Bodies”.
You have referred to the deceased woman as being of African descent. Was Mr Medson Godfrey not of African descent?
Sorry my kinsmen this is the river where i learned how to swim in my chidhood days crossing from m’bawa to namalomba for pleasure…MHRIP
What I meant was a call for center to take on pipo in this time of emergency. osangoti chokani
Yakwiya Ndimizimu,uchimo Wachuluka Padziko
Police yopoyira
Mmmmmh Balaka
I think masoapatali ndiwe kape kwambiri. Unakula ndi moyo odalira. Chilichonse basi Boma litipangire? Tonkha sitingangoona kuti malo ndiliwa siabwino ofunika ndisamuke? Anthu opusa ngati inu ndiamene mukupangitsa kuti Malawi asatukuke. Chilichonse atipangire, iweyo ukutani
Che Masoapatali mudziyakhula ngati wanzeru. You mean boma should live your life. People have to move thats a must dont wait for the government. Moyowo ndiwandani kodi?
Aziyankhula ngati wa mzeru mukumuziwa inuyo. Mwina mzeru alibe