Email a copy of 'BB fans threaten 'tit-for-tat' action if Nyasa pull out sponsorship: Champions issue gagging order' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'BB fans threaten 'tit-for-tat' action if Nyasa pull out sponsorship: Champions issue gagging order' to a friend
Justice Link executive director Justin Dzonzi has advised legislators to avoid taking to ransom government on issues of budget allocations...
NYASA JUST INTRODUCE THE CUP FOR SUPER LEAGUE TEAMS
Just sponsor the cup for all teams in Malawi, BB should sort out their problems first NYASA CUP for MK100 Million a year
kodi mwata anthu inu kodi teamyi mukuifula zabwino?tachitani manyazi
Enawo angochoka zikuwanyasawo amusiye sam chilunga ayendetse
team ndiyokanika iyi, komabe timaikonda
Am Bullets fan bt ummmmmm team iyi ndiyokanika eishee kodi munakhala bwanji mbava inu? Koma tikangoluza sponsorship imeneyi ndinthu Bullets sizapezanso mpaka Ambuye Yesu azabwela. Kodi enanu bwanji osangopuma bwanji? Musiyeni Sam Chilunga plz.
a Sapota ndinu mbuli zedi mupanga boycot ma cigarett ?! This guy is an embarrassment to the club and the nation. I urge Nyasa Company to pull out quickly because this is a team of savages they do not need sponsorship at all. Infighting is purely to steal money auponda ! Leave Big Bruts alone !
Bullets supporters pls behave
mxiieeeiw boycoot with your 2 kwacha
ZAVEKA MADZURO POMPANO KUTI OFFICIAL AMENE WAITANITSA EMERGENCY MEETING MAWA AKAKANGOYEREKEZA KUNENA KUTI ASIYA KUTHANDIZA BULLETS AKUTI AMUKHAPA APO BEE ACHOKE MDZIKO MUNO KUNGOYEREKEZA KUMAKHALA MOMMUNO ZAKE ZADA BASI AKUTERO MA SAPOTA ENA A BULLETS KU NDIRANDE NDE ANTHU AMENE MULINAYE PAFUPI MUMUWUZE ZIMENEZI CHONDE CHONDE