Email a copy of 'Be Forward Wanderers entertain villagers at Ngokwe ' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Be Forward Wanderers entertain villagers at Ngokwe ' to a friend
Catholic Church are continuing their observance of the Christian Passion today, Holy Saturday, and Easter Sunday. Thousands of Catholics from...
timu yathu ya manoma timaikonda. zivute zisavute mpaka kale. manoma woyeeeeeeeeeeeee!
pepani abale,if our Noma played with remote team Ngokwe as such 0-0 don’t blame the ground.We must improve!!!! neba asativutenso,maybe invite Ngokwe at Kamuzu stadium
Kod mmamidzimu akumakafunamo ngunda yamphamvu kapena?? Kkkkkkk
Koma chitimu ichi abale achachachachacha.. Iliponso Ina kuno kwathu. Chakachino ndithudi, wachikopa pamwamba timikjapwira. Uyoooooooooo…udziwanso.
Chitimu Ichooooo
good development by Nomads though they played on a Potato Ground.
Kkkk………… Koma manoma wamkaka basi chakachino amasikini ali m’madzi ma vendor a CHINGAMBWE mukumva bwa!!! kuyabwa
It’s sad that the whole village cannot afford to have a proper football pitch. Is it difficult to dig up a pitch, level it up and then grow some grass on it? ku Malawi bwalo la mpira upeza kuti ndi lopanda kapinga kapena ngati pali kapinga ndiye kuti likhala losatchetcha. Ulesi ndi kuzolowera zinthu zosakhala bwino. Mbuzi za wanthu
that’s my manoma. team ya anthu ozindikira. osati zinazi tikuwonazi, daily anthu kusiya ntchito.
u know is 100%