Email a copy of 'B’ella movie to screen in Malawi secondary schools' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

6 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
jigidijigidi jaba
jigidijigidi jaba
9 years ago

A Hoitty kutereko muli mugulu lopangidwa brainwash kuti ndevu ndizoyipa. Kuteroko Mulungu anapepela pomupatsa munthu wa mwamuna ndevu? Ngati zili choncho ndiyetu amuna onse ndima Talibani kungoti ambiri amadzibisa pochotsa ndevu zawo. Osamaganiza mopusa chonchi pazinthu zokhudza chilengedwe chomwe mulungu atamupatsa munthu anawona kuti zilibwino. Kutengeka ndi zikhalidwe zomwe zimapangitsa kuti anthu ayambe kudana ndi chilengedwe chomwe mulungu anawapatsa kudzakupangitsani kunyoza Mulungu. Ndikhulupilira kuti inu ndinu Nkhiristu. Ngatizilichoncho ndiye musiyiretu kutsata Yesu ndi ena onse okhudzidwa ndi za umulungu a m’Bibulo, monga a china Mose, Abraham, Yesu amene, Yohane M’batizi, poti onswewa anali ma Talibani andevu zawo zakathithi. Tamagwiritsani ntchito… Read more »

Selection
Selection
9 years ago

Please,do not waste our time as we are busy preparing for final exams!!! Here in Malawi,one needs to be selected and not as other countries!!!!

CK
CK
9 years ago

Zachuluka pa Malawi ndi nsanje. Its not about money, these guys have been all over the world and are still traveling, this movie good for students

Mbowe Mulambia
9 years ago

This is fund rising at its best a Malawi anachangamuka.

hoitty
hoitty
9 years ago

Aphunzitsi a dziko liti amakhala ndi ndevu chonchi? ku School of Taliban kapena?

Kwangwagwa
Kwangwagwa
9 years ago

Kodi mumayamba project mulibe makhobiri? Shupit time wasters.

Read previous post:
Sankhani Mkandawire makes u-turn, still with Bullets

Big Bullets defence pillar Sankhani Mkandawire has reversed his decision to quit the club and has returned to the champions....

Close