Email a copy of 'Bernadetta Mlaka Maliro to launch debut album ‘Yahweh’ in September' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

18 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Mtunda
Mtunda
8 years ago

Good luck! will be there once u hit boma park in Mzuzu city.

Zagona
Zagona
8 years ago

Malawi @ 51, everybody wants to be a gospel musician!

Predominant
Predominant
8 years ago

Nawenso Beatrice ndi galu ngati amuna ali agalu mumavulira dala zanu zimenezo akuvulanidi ndithu agaluwo muona ndithu.

Beatrice Mangochi Mgaliba
Beatrice Mangochi Mgaliba
8 years ago

Komadi in general my fellow women when we are empowered and financially sound lets respect our husbands in all areas kaya ku bed kaya kuwaphikira etc osati kuyamba kuwathawathawa and start enjoying with other men but only come back to our husbands who may be less privileged zikatisokonera.Anthu amaonatu and amuna ndi agaru amangouza aliyense za amene agona naye palibe amasunga secrets!!!!!!!! Tizalira amene akutinyenga akathiwa kubwerera kwa azikazi awo and amuna anthu nkutikananso and chuma nkuthaso wakumva wamva

kaya
kaya
8 years ago

Nawenso commentanto V Tembo ndi mbuzi yopanda mano comment yako ya ma capital letters unapita college yakuti, ya gogo wako kapena tikamalemba pa nyasa sitiona za chizungu kaya makoma kaya spelling malinga timvanepo apa after all these days ma phone athu amtilakwitsa tikalemba zina iwo alemba zawo ndiwe just take the sense brother

Bwande
Bwande
8 years ago

Interesting how common these days it is that people kick start a music careers way in their forties and some even older. Honestly I am seeing this only here in Malawi. Last time it was Shanil Muluzi akuti gospel album. Pano ndi izi. Anyway poti ndi za ambuye tiyeni nazoni

Ondira
Ondira
8 years ago

Ambuye anadalitsa banja lanu pokuikani pa umpando wa u MP. Inu mwayamba kuderera mamuna ndi Mulli nkwenkwere nkhwekwere ntown zosapatsa ulemu zija. Mulungu ali ndalakwitsa, 2014 kukulandani u MP. Anali ndi cholinga kuti musinthe mumange banja lanu. Sinthikani pa choonadi other wise Mlaka akanakhala ngati Amuna enafe,,, bwenzi pano ili history kuti you were once Mrs.

VIYAZI TEMBO
VIYAZI TEMBO
8 years ago

ZIZUNGU ZA KUMALAWI! MACOMMENT AKE OPANDA COMA, FULLSTOP, ZOVUTA KUMVA.

...
...
8 years ago

Jealous ili pati apa?
Pitani kwina kuli konse pa dziko lapansi, LAUNCHING ndi KAMODZI basi.
Sizikugwiridzana ndi jealous idiots.

ma hope a stella gwengweya
ma hope a stella gwengweya
8 years ago

koma ndi machine

Read previous post:
Rev Maulana re-elected CCAP Blantyre Synod SG: Chimkwezule is spiritual father

The Blantyre Synod of the Church of Central Africa Presbyterian (CCAP)  has elected top synod officials with Rev. Alex Maulana retaining...

Close