Email a copy of 'Bogus PSLCE candidate arrested in Chilomoni' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Bogus PSLCE candidate arrested in Chilomoni' to a friend
Hardly two weeks after jointly handing over a classroom block at Chitipi LEA School with the Rotary Club of Northampton,...
Wat wil b the possoble jugement
Wasala Kondwani Nankumwa nayenso zikumveka kuti akugwiritsa ntchito certificate ya m’bale wake.
zazii mwanayo angayankhe chani, wapha munthu? osalimbana ndi nkhani zenizeni bwanji palinso nkhani apa
Nice for arresting this young crook.Ndi ma crook azizavuta kutibera mtsogolo.Mayeso amalemberana?I thought Maneb introduced photo ids even to std 8 people?So you mean the invilgilator didn’t the id for the sitting student?
zachamba bas iyah mtuzi wanu apolice mwapeza potchukila ife tzt ntchto mukuigwla zopusa bas
A Malawi akudikira mpaka pano kuti nkhani yija ya K92billion yitha bwanji.
Kodi mayenso ayamba kulembedwa kopanda ma invigilators pano eti?ngati yankho ndi ayi,nawonso akwidzingidwe akayankhe bwino nanga ntchito yawo ndi chiani?
stupid policemen. Why cant u arrest the real thieves. The DPP and Mulli are stealing from us in broad day light. Leave that poor15 year old alone. U r failing to arrest the real thieves. Chokani apa, agalu inu.
There is nothing like leave him alone when it is a criminal offense. Malawi is called a failed state because law and order is not there.
Ntchito za anthu a pakati ndi kumwera kuba basi