Email a copy of 'BT derby win gives Bullets back the bragging rights over Nomads: Malawi TNM Super League' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

40 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
nneka
nneka
8 years ago

man of the match amatenga amene wasewela bwino kuposa anong`a,jafali,salad,chichukepo,chamba(fodya)ndi wina aliyese amene anavala zofiila. noma for life!!!!!!!!!

Allie Kaleyah Hamees
8 years ago

The pples team aliyese amangodziwila2.enawa ndi anawoti talera tokha koma mwano 2mch.

murray
murray
8 years ago

Viva Maule…… Koma zoona man of the match kuchokela ku Team yoluza? kupangaila kuti asaluze zonse kapena chiani inuyo a ujeni? ………………….kkkkkkkk

Totolitotoli
Totolitotoli
8 years ago

Bullets ndi deal, Wanderers mpira wao ndi wapakamwa mu ground ooooh! MAULLETS NDI TSIDYA LINA ,saizi ikusowa,ma bankers ana,wanderers mn’gono wake wa Silver gosh!! nanga titani? tidzingosewerabe ndi makandawa.

martin gonda
martin gonda
8 years ago

Nyerere ndi nyerere basi

sain it like it is
sain it like it is
8 years ago

how does the man of the match go to a losing player?

bbsupporter
bbsupporter
8 years ago

INE BAMBO BIG BULLETS FOOTBALL CLUB NDIKULONJEDZA LERO KUTENGA BEFORWARD WANDERERERS KUKHARA MZAZI WANGA KUYAMBIRA LERO MPaka imfa idzatilekanitse. Tithandidzeni mlungu.

ZZ Junior
ZZ Junior
8 years ago

Za chamba basi. Anakuwuzani kuti Man of The Match amachokela ku team yoluza ndani?

Chande
8 years ago

I LOVE MY TEAM BB,NOT NYERERE,KANYERE KAKAKUMANA NDI NJOVU,NJOVU YAKAPONDAPONDA SIKANAWONEKENSO KA

Palichina
8 years ago

League simungatenge inu! mr nyamilandu muyimenso wanderers more fire!

Read previous post:
I’m not in exile, says Joyce Banda: Hails Britain for support on Malawi cashgate probe

Former Malawi president Joyce Banda has said her nine-month absence from the country does not imply that she is in...

Close