Email a copy of 'Bullets and Wanderers draw 1-1 in Blantyre derby: Malawi TNM Super League' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Bullets and Wanderers draw 1-1 in Blantyre derby: Malawi TNM Super League' to a friend
The long awaited Blantyre Half Marathon is all set for Sunday as Malawi’s competition starved athletes get the rare chance to contest....
Nyelele ndi akamuna ,uyundi Amos watsala Nakamula(nebaulimba?)
A bibi mukunama, chaka chino mu bibi dwadi . Nyerere woyeeeeee
anthu ozolowera kutibulidwa ndi choncho. posachedwa pompa takukhadzulani 2-0 koma mwano osasiya umenewo sindiye umbuliwo. mmalo momadandaula kuti chikutitsata ndi chiyani busy kutukwana. za mpira zomwezi kapena zina? aaaaaaaa tionana second round.
BB ndi akatundu olemera ngati mchenga
Zitisatirani a Ndudu BB inu chaka chake ndi chino. Blue Eagles ili panambala one, Noma panambala 2 pamene Chingambwe chili pa nambala 3.
Mwasitha mtundu wa jins auzeni masapota anuwo asithenso flag zinthu zakumvutani
Agalu a ndudu zonyasa inu, osasamba, onunkha, sukulu zero, zikwanje zokhazoka, munya chaka chake ndichino, ndi ndudu zanu zonyasazo
Noma 4lyf
@ Samson wa Noma Bullets si agalu,agalu ndi family ya kwanu + team yako ya noma yo + executive yanu ya noma yo + ma sponsores anu a b4wd wo shupit,ndi za mpiratu izi si za kunyumba kwako ayi.Kodi dzigoli za penarty zimakhala ku MW kokha fotseki!!!!! ndikupatse assignment undiyankhe kuti team yakoyo inachinya liti Nyasa Big Bullets? mxiiiiiiiiiiiiii
KUNGOTI ABB FODYA AKUYALUTSANI MPAKA KUGOLETSA PA PELNATY MKUMATI MWASEWERA BWINO TIONANA SECOND ROUND AGALU INU.