Email a copy of 'Bullets beat Zimbabwe Caps in Zambezi: No trophy presentation' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Bullets beat Zimbabwe Caps in Zambezi: No trophy presentation' to a friend
We all used to love TVM back in the 90’s and early 2000’s, before it changed to MBC, after all,...
Mukamamva kuti chipongwe ndichimene Mwachita apachi, chipongwe chopanda mkhalidwe. Pochita zinthu zanu mudzichita mchilungamo.
Koma a FAM ,Kelvin Moyo ndi enawo anene bwino za Zambezi Challenge Cup.Chifukwa ninji kunena kumapeto a mpira kuti siunali mpikisano koma friendly chabe?Kutitola eti?Dziko lonse timadziwa kuti uwu ndi mpikisano wa chikho,koma from nowhere basi mukuti inali friendly? Aaaa! adada Moyo pamoza na wanyinu tiphalireni makola tipulike.Kodi ma coach nawo samadziwa zimenezi?Nanga techinical zonse mbali ziwiri? Ma player nanga?
Northerners are dominating look at the scorers; Fischer Kondowe, Chiukepo Msowoya and Ishmael Thindwa all from the North sha! north ndiribe nayo mawu ndithu timakusilirani. By the way I hear that it was a frendly match what is happening? Zambezi don’t take clubs for granted.
BB kuti wawawa!
Zili mushe ele, aaa zwakadiko chamwali Bullets inonesa. Kkkkkkkkkkk tsono coach wa Caps you say as we are going to Sudan we should take referee, what do you mean? Mukuganiza kuti anatikondera? Ndi mwanotu umenewo.
tikumwabe wamkaka mpakana kale kale majelasi bwnji amalawi asiileni ndalamazo sikuti mutengeposo agwilitse tchito ulendo wao
A Silver amati paoneke wamkulu pakati pa iwo ndi BB, ndiye iwo anazuzundidwa 2-0 pamene BB yazuzunda CAPS 2-1. Mizozodo ndi iti pamenepa? Manyazi bwanji ndi nkhwidzi zanuzo.
No any other team in this country than Big Bullets.kodi team yabwino ipose iyi? Jelasi bwanji? enanu idakumenyani yomweyi musathe mau.Bullets kundivetsa kukoma ine!
pena muzichitako manyazi, chisoni nkumakupezani iliri
Big Bulletsyi inu nkumati muitengere ndalama, ufiti kapena chani? mmmh zanjeza
asiyireni anzanu nsanje isamadutse apa nanuso aboma malo moti tizimva kuti mwawaonjezera ndalama mpame tikumva kuti mukufuna 25per cent kulakwa.
This is a stupid article! You were supposed to tell us why there were no trophy and prize money presentations.