Email a copy of 'Bullets blow away Mafco to re-launch title defence, unbeaten: Malawi TNM Super League' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

28 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
emmanuel
emmanuel
8 years ago

bullets woye

Alex Grey Ndaipa
8 years ago

BB wawa

Chifundo
Chifundo
8 years ago

Game inamenyedwa kuti? chithunzi cha Fodya akuvinacho musatinamize, ngati munalebe chinthunzicho munakangolemba nkhaniyo mwamva.

bambo
8 years ago

Kudangira nkhufika yayi abullets, Timusanganinge muthowa. Noma wayeeeeeeeeeeeeeeee

Big papa
Big papa
8 years ago

mmmmm mafco imaona mdima after nyerere zitawapengesa.

Nyenyezi
Nyenyezi
8 years ago

That’s the People’s Team I know zinazi ndiminyanya, opanda sponsor but praying classic football and earning 3 points pompo pompo away for that matter is not a mini achievement. Thumps up to our Headmaster Yamikani Fodya the free-kick wizard. Neba ndiye wamwa wamandimu wopananso sugar chisangalalo chonse cha carlesberg cup kuthera pompo. More fire maule pamenepo ndiye mwandiputa moti sapota mapeto im sending many sms just to support you guys.

Wangandiyemweyo
Wangandiyemweyo
8 years ago

Mwati Bullets nkumadzulo? Kale kamene kaja! Masiku ano ikumawomba nthawi ina ili yonse – mmawa, masana, madzulo ngakhalenso usiku. Chipolopolo sichiwona nthawi abale. Enanu omwe simunakumane nayo, watch out! Ifetu tidakamwabe wamkaka. Tsoka aneba. Ayi pepani, komano pamaliro anuwa sitikhalapo tikuthamangira kukadyanso wina yemwe SULOM yatikonzera.

Hardson
8 years ago

Eigh…. Coaches! Tapqngani za kupsya please tisamangodalira ma free kick tsiku lina tidzakodza nazo zimenezi aaaa. Any way big up boys you have made us proud. Mulembe nsanga nsanga ya Be Forward tione kuti zili bwanji mwina enawa akutinamiza zoona neba angalize…. Iyaaa ndi CIVO? Osatheka CIVO yoti inatopa dzuro ayi aa.

Immaculate
8 years ago

Imagine Neba Civo yamukutumula akuti pa home waiwala neba kuti anasamukira ku Balaka

ZZ
ZZ
8 years ago

BULLETS POINTS SHOULD BE THIRTY NINE AND NOT THIRTY FIVE

Read previous post:
K90m Malawi TNM Super League 2nd round launched with hype

Business came to a halt at Dwangwa trading centre in the lakeshore district of Nkhotakota on Saturday, 12 September 2015...

Close