Email a copy of 'Bullets’ Chiukepo, Chaima to wait longer for CAF: Ramadhan not panicking' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Bullets’ Chiukepo, Chaima to wait longer for CAF: Ramadhan not panicking' to a friend
Businessperson and cashgate suspect Osward Lutepo has been certified medically not fit for trial in the various charges related to...
All the best MAULE osafooka forward ever backward neeeeeeeveeeeeer
Amalawi mavuto anu ndiamenewa, ngati sitili limodzi osalankhula zambiri, wathu ndi mulungu basi.
Maule tili pa mbuyopo all the best timakukondani let them talk sazafikako ku Comoros makapewo asova ndi iwowo. mwaaaaaaaaa maule.
TSOKA LIKALIMBA AMAKULUMA NDI MWANAPIYE
PEPANI NEBA PEPA.
Anthu Opusa Inu Munayamba Kalekale Kukhala Ma Administrators A Mpira Koma Osadziwa Malamulo A Caf. Kondi Uzikhala Ndi Nthawi Yowelenga Wamva? Osamango Chita Ma Bizinesi A Ukhuluku, Umawonekera Poyelatu.
Even kondi is a nomad koma chifukwa choti kuli mbuzi zokhazokha ku bullets akudziwa kuti easy money apeza its unheard of in the world team kumapanga cost cuttings achoncho!timu yamabulutu game yoyamba yomweyi muona ma result ake musova!
Hahahaha team ya mbuli
Vuto lakumalawi ndilimenelo kukhomererana basi but god is still on our side we ll make it.
A Msungama Ndi Afote Imene Mukuchitayo Si Administration Koma Kuba Inu Mungasiye Treasurer Kutenga Vice Ngati Akudwala?Shame! Inu A Fote Mukuti Munali Ku Chanco Munakatani?Kulephera Kuchita Confirm Ndege Koma Kuzunglira Dziko Lonse Kupempha Inu Ndinu Treasurer?