Email a copy of 'Bullets claim back-to-back Malawi TNM Super League title' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Bullets claim back-to-back Malawi TNM Super League title' to a friend
Lilongwe based golfers Thakor Sanjay and Mina Mkandawire had every reason to brag about in the corridors of Lilongwe Golf...
bb iyenera kumakasewera UEFA Chifukwa ndikomwe kuli masaizi awo,kumalawi kuno azingo pwetekesa miyendo
Coach wa malawi awonetsetse anthu amene akuchinya mu s/league, kuti adziyamba kusewera mu (nation team) koma osayiwara jafalli chande ndi tondo ameneyo.
Tikumwa wamkaka tsiku lililonse, ena mwangoti mutu bi..iiii.
BB NDI MOTO BASI olo wina afune asafune une kuwecheta basi o o o o o amai ndi abambo anyamata ndi asungwana ndinaiwala NA BIG BULLETS AAAAA Kantera
Bullets Ilibe Kuimitsidwa Kaya Tinyerere Timangoponda Ife 4 We Are The CHAMPHIONS!!!!!!!!
League tatenga basi
BB chaka chino ligi ili manja basi
MPAKA MVULA NKUYAMBA MUSANATENGEBE CHIKHO!!!!
Tionana next yr. Tizaone ngati mungazanunkhenso ligi@@@@@@!
Be4ward directing manager amvekere “ife wanaziwa kale kuti Lali lubani sathandiza, bola bullets yemwe uja koma Nyau Milandu anatisokoneza aaaa nanga onani olo malonda athu agalimoto angayende atiyipitsira mbiri.”