Zona Bullets ndi brand yaikulu koma zomangosewera ma bonanza chisawazi musiye,mukufuna kusewera caf ndiye ma player apuma nthawi yanji caf imayamba january(ndichibwana chichikulu chimene mukuchitacho osamakonda ndalama choncho 1m or mk.5m ndichiyani bullets yapeza ndalama zambiri over 80m kusamala inali ndalama yambiri imeneyo kom zibwana zikuchuluka)
Chokazinga
9 years ago
I will never take ur Chairman Kondi Msungama seriously he is always in the media promising.He is toking too much whatever he dreams,he promises his supporters.Kondi please slow down your pace you are driving too much,avoid toking to media before you implement.Auzeni kaye masapotazi anu mmene mwayendetsera ndalama za BB mu season yangothayi. Mukwauza masapotazi anu akuti mukufuna mutenge ma players athu ku Wanderers musayelekeze,mungoti ichi mwanena mwanena timve ziti.
Msungama’s chairship has made bullets what it z now-a real pple’s team. The chair had to weigh d cost effectiveness of every undertaking. C now what? Mind u, he can also comfortably accomodate other peoples views. Instead of takin d team only 2 RSA he’ll take it 2 d whole African continent. Bwanji pamenepo man?
Palibe amene angapeleke ndalama ku bb atafuna ngati tomato anthu akuba inu.
good lacky my son am old now
BULELTS MKAKA MKAKA
Zona Bullets ndi brand yaikulu koma zomangosewera ma bonanza chisawazi musiye,mukufuna kusewera caf ndiye ma player apuma nthawi yanji caf imayamba january(ndichibwana chichikulu chimene mukuchitacho osamakonda ndalama choncho 1m or mk.5m ndichiyani bullets yapeza ndalama zambiri over 80m kusamala inali ndalama yambiri imeneyo kom zibwana zikuchuluka)
I will never take ur Chairman Kondi Msungama seriously he is always in the media promising.He is toking too much whatever he dreams,he promises his supporters.Kondi please slow down your pace you are driving too much,avoid toking to media before you implement.Auzeni kaye masapotazi anu mmene mwayendetsera ndalama za BB mu season yangothayi. Mukwauza masapotazi anu akuti mukufuna mutenge ma players athu ku Wanderers musayelekeze,mungoti ichi mwanena mwanena timve ziti.
God is able we indeed going to get sponsorship
Its high time sponsors started sponsoring a winning team and not a violent team just bkoz some1 above z a staunch supporter of that particular team
And this sponsorship is kuku matches by Jussab to the tune of k30 million which is better than none mark my words
Msungama’s chairship has made bullets what it z now-a real pple’s team. The chair had to weigh d cost effectiveness of every undertaking. C now what? Mind u, he can also comfortably accomodate other peoples views. Instead of takin d team only 2 RSA he’ll take it 2 d whole African continent. Bwanji pamenepo man?
The peaples team