Email a copy of 'Bullets fan wins Plasma in Nomads promo' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

9 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
peter chitete
9 years ago

nyerere mpaka kufuna kuguritsa timu ku bb mulibe nazo ntchito zothandiza team yanu nonse inu masapota anyerere mwina mukupanga nayo manyazi ndi performance ya chaka chino

fyson kanyengo nkhoma
fyson kanyengo nkhoma
9 years ago

Zawonetsa kut anthu amakonda kwambri mpira timu yawo ikamachita bwino.nyerere zilipo koma ndi mvula ili kunomako zalowa kaye.

duduzi
9 years ago

Nomads ndi team yaanthu onse ngakhale a Bullets amayifuna nayisilira nchifukwa chake amasapootabe pozera ku mpikisano wa sms.

Komanso ndiyachilungamo ndiponso mtendere ….chifukwa anakakhala nebayu, anakapereka Plasmayo atawina wa Noma? MaPale…? Mufunse?

Nalo Banda
Nalo Banda
9 years ago

Makosana, posanama Mike Butao akuyesesa. Chikhalireni bwana Mike GS wa mighty ma Norma akulozeka. Amenewa ndiye ma GS ofunikila pa ball olo ku FAM kumene. Zabwino zonse bwana Mike ndi ma Norma onse!

iphani mudye
iphani mudye
9 years ago

neba bullets yakuzunza mpaka kukutengela prasma ulipompo uyisovenge

Oliver chiwaya
Oliver chiwaya
9 years ago
Reply to  iphani mudye

Ma sapota a noma samiyitsata team yawo, nanga kumakawina wa bullents inu mulipo?

Patriotic
Patriotic
9 years ago

Ma palestina amenewo, mpaka kulowelera mu nyerere family

banana kara
banana kara
9 years ago

Mwawadyera ziri zawo kkkkkkkkkkkkkkkkk

Danny
Danny
9 years ago

Zili bwino mayi pamenepa .

Read previous post:
Malawi fuel shortage fears dismissed: Mera says no panick buying

Malawi Energy Regulatory Authority (Mera) has dismissed fears that country faces imminent fuel shortage. Mera chairperson Lyton Zinyemba said the...

Close