Email a copy of 'Bullets get revenge on Wanderers: Malawi TNM Super League' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

72 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
west bouy
8 years ago

zimatere zimatere bwenzi zikoma kudu kudu kudu ng`omatu zimenezo

Wa Maule weniweni
Wa Maule weniweni
8 years ago

Comment # 69 – Eee ndimmene zimakhalira kodi eti? Ayi tamvera inu. Nde mukatero sing’angayo mumampatsa zingati? Mwina nafenso tingapite konko tidziluza nawo. Komabe ife a BB tilibe nthawi imeneyo ife wathu ndi Mulungu (Yehova) osati mafano (Baal) anuwo. Ndipo mukanakhala kuti mankhwalawo akukupindilirani bwanji osaigaira Flames idzatengeko World Cup? More fire BB.

yazula
yazula
8 years ago

pepani a Kananji,pepani a Nyamilandu,pepani a Madeira,pepani a Yona,pepani a Zidana,pepani a Melvin Nkunika ndi nonse anafedwa,chapha malemuwa ndi thiraki yonyamula clinker ndiye malirowa palibe kuona nkhope coz sikuoneka nkomwe. MAULE amapamantha zedi ,aliponso wina?Tinanenatu paja kuti 4-0 ya Al-Hillal ija munya nayo nonse kuyambira iweyo neba lero siizi? Pali mau,ngati sukumvetsa kachotse BB pa # 1 ubwerepo iweyo

zanga phee
zanga phee
8 years ago

Zinthuzi zikuwoneka ngati zazing`ono, palibe wa manoma amene anapita kwa ayaya.
amene anapita kwa msing`anga ndi a MAYI MOFFAT ,Mzimayi wa ku Lilongwe uja amati Manoma akawina Carlsberg avula uja.
A Bullets akumaika mankwala mmagate olowera mu stadium , komanso amalemba mayina onse a maplayer a timu ina mkupita nawo kwa msing`anga kumene msing`angayo amawamanga miyendo ma playerwo ndikuwapatsa chidima kuti asamawone bwino pagolo., ndipo amawauza kuti mainawo akawaike pa centre poyambira mpira.
kunja kuno kuli Mulungu mudzafa imfa yowawa takudziwani.

waseme
8 years ago

M’ngoni weniweni nawenso wasanduka ref? Osangovomera kuti NEBA waluza. Mumuwuze Yona wanuyo kuti asiye zomabetcherana maphokonyorewo. Ameneyo ndiamene akukupweteketsani. Maulee Woyyyyeeeeeeeee.

ule in mozambique
ule in mozambique
8 years ago

ine kumva yogati nthupimu, wishing i ‘d b there 4 myself to celebrate with timu ya mfuko.

madzi apita
madzi apita
8 years ago

Manoma mwafa basi mukabweze ngongole kwa Ayaya kuti muyambe kuwina ndiye poti ndinu osamva mukhala choncho

REAL BULLETS FUN
REAL BULLETS FUN
8 years ago

Brava maule

Mr.Bambo
Mr.Bambo
8 years ago

Moni moni moni a Elia Kananji.Kaya mukumva bwanji mthupimo?

Wachinyamata
Wachinyamata
8 years ago

Bravo maule zangoonetsa kut neba ndi amene amayambitsa ziwawa akuluza, ife tinaluza carsberg kma anthu sanagendedwe

Read previous post:
US granted 115 visas for Malawi delegation to UN: Mayaya hits at Mutharika advisors

United States embassy in Lilongwe granted 115 visas for Malawi delegation to United Nation in New York, confirming that the...

Close