Email a copy of 'Bullets hope Nomads target Chiukepo will sign new deal' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Bullets hope Nomads target Chiukepo will sign new deal' to a friend
During the demonstrations to draw attention to the various economic problems rocking Malawi, John Kapito, the Executive Director of the...
Achiukepo,talk with nyasa bullets.Dont go to nyerere plz.Zikakuluma.Nyerere ndh team nanu a chiukepo?Ngati wasowa team,come here nizakakupe team.Bullets yomweyo,kambilanani.Mzakwacha pretoria.+27731440799.
@mulhomwe wankulu….Zoona afere zimezo akupatsidwa peanut nayenso akufuna greener pasture mmene inunso mwasinthira ntchito mumakampaninu………….kkkkkkkk
Go to end miserably
Wakula uyu asatiwawitse mutu,wasintha chani ku bullets, tinagulitsa gaba iwe fulakishoni yako ndi chani kwa gaba? usatidwalitse mimba.kazivaya
Chiukepo choti ukumbukile ndichoti ife Anoma ndife omwewo tinkakunyoza Bullets itakutola patchire utachoka ku Mozambique. Tinalankhula zambiri mbiri zokunyoza iweyo pamodzi ndi Bullets, nde lero Bullets yemweyo yakusambitsa bwino bwino wayamba kuinyoza? Tinkati a Bullets atola gogo opanda mano nkamwa lero poti wamela mano wasanduka kamnyamata? Pena muziganiza bwino bwino inu ma player athu….
Bravo Chiukepo football is a short term carrier make hay when sun shine
Chiukepo wants to use Nomads to get a good deal at Nyasa bullets
Ano simasiku olandira dola yonyenyeka bravo chiukepo footbal is ashort term carrier demand more frm them basi
Chiukepo Usalole Contract Ya Ndalama Zochepa Paja Sulumba Walandila Zake Ndiye Iwe Ndi Sulumba Dolo Ndi Ndani? Akupase 10 Grant Wamva Apo Bi Lowela Ku Nomards Konko
ine sindidandaula za chiukepo,akanakhala sulumba