Email a copy of 'Bullets need K12 million for Sudan game' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

38 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
baggio
9 years ago

bb ipita

OGADA Bambo a MUYUDA
OGADA Bambo a MUYUDA
9 years ago

The Fombon game deserve to cater that little amount to fulfil the trip to Sudan koma basi mwaba dollar zija. BASI khalani musapite. mbava

nyasa boy
nyasa boy
9 years ago

Amayo munaziyambilanji mulibe ndala kupempha mpakanaliti mukakhale Ku ofanikeya muzikalandiranawo chithandizo chochokera mmabungwe akunja

kkkkkkk
kkkkkkk
9 years ago

Wasanje utopa wenkha BB ipitiriza kupanga bwino ngankhale tipezane ndimavuto poti pamene pali Mavuto mtendere ukubwera dikira uwone tikunyamula Caf mumalere iweso uzankhala woyamba kusangalala

Abudul latiff
Abudul latiff
9 years ago

Basis musipilila a bb ndalama zopempha ndi choncho

wolangiza
wolangiza
9 years ago

zowonadi munthu akamachita bwino ambiri samufunira zabwino .tawonani apa amariwongo angokamba za BB mumaro monyadira BB kuti yikusangarasa dziko la marawi .chifukwa pa malawi palibe timu yozipereka pankhani yamasewero .ndiye wina ungoti nyoooo uyerekeze uwone zomwe anawona azako ku nsanje

Lloyd Matambula
Lloyd Matambula
9 years ago

People we are all Malawians lets support BB bez this are international games. They are carrying Malawian flag……………………………………..aaaaaaa!!!!!! shame on you

zanga phee
zanga phee
9 years ago

Mungoti mukufuna ndalama , Kodi game ya Saturday munapeza ndalama zingati, tiuzeni mwachangu, kumangodalira kupempha basi , neba zanyanya tsopano.

chilombo
chilombo
9 years ago

Koma Bullets nditeam yosauka guys,kupempha ngati amaskini. Game iliyonse tizisonkha?

Phodogoma
Phodogoma
9 years ago

Kondie Msingama is likely to be a poor mathematician or he is a trickster who steal in broad day light. I mean how does he come up with figures for CAF? Who is his accoutatant? Shame on you Kondie. He estimated 30 meter for the trip to Comoros. Now he is estimating only 12 million for a trip to Sudan. I expected him to mention around 100 million. Unfortunately if you give them 12 million what you hear tomorrow will be that the guys have left by bus as they will board a plane in Uganda.Dribbling of this kind can… Read more »

Read previous post:
Seodi White on CNN- ‘No ifs or buts’: Child marriage needs to be abolished in Malawi, once and for all

About 15 years ago, I was doing research on inheritance laws in Malawi and their impact on women. Part of...

Close