Email a copy of 'Bullets, Nomads clash in Mayors Charity Shield' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Bullets, Nomads clash in Mayors Charity Shield' to a friend
One of the prolific coaches in the domestic football scene, Nicholous Mhango of Moyale will step down in his coaching...
Ndikuva chinsoni ndineba.tabyaso mwa noma. Bb zikuntheka enanu mudikile zaka 7 chifukwa apatayamba uyipota.
Timwa wa mkaka , ..noma woyeeee…
good pa good.tiye kakhwasule kanoma,katsuke mkamwa.i like bullets abale.
A BULLETS TIYENI TIKAGWIRITSE NTCHITO ONSE OMWE SADAMENYE SUPERLEAGUE
Bullets do not have mercy on them!!!
noma woyee tamwanso wamkaka
I think we need to rest our footballers. That’s why it is difficult to play well in important matches because they are burn out….
Neba waphedwanso pa 13 pano
bolatu epac nanga noma za zi
Anzathu ku Blantyre zikuyenda. Munasankha mayor wachinyamata, wangwiro, wophunzira, wamfupi bwino, woyera komukhala ndiponso wokonda mzinda wake. Kuno ku LL ndiye eeish, uyu ndiwofunika kukhala mayor wa kudambwe basi. Guyz tisinthane bwanji?
HAHAHAH MPAKA WA KU DAMBWE?
kodi ma player athu sazipuma basi mukungowagwiritsa ntchito ngati chida chopangira ndalama pomwe ndalamazo sazionanso,player amayenera kupuma kuti season ikubwerayo asewerenso bwino thupi limatopatu(kodi inu akuluakulu a bullets ndi noma za mpira mumaziziwa bwino bwiono? tiyeni tisamale ma player athu kuti atigwirire nthito yabwino nthawi yaitali,,,….ngati matimu alibe ndalama tisazuze ma player aiii….