Email a copy of 'Bullets, Nomads gearing up for Malawi Carlsberg Cup final: Captains speak of the showdown' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

46 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
WANDAWANDA D
WANDAWANDA D
8 years ago

NYERERE WILL CARRY THE DAY

ayothi
ayothi
8 years ago

B means bullets. forward means pasogolo. B FORWARD MEANS pasogolo ndi bullets. BULLETS 3 AKAMADZI 1

Bambo atuwiri
8 years ago

Eliyaaa! Pemphela kuti moto utsike kuchokela kumwamba uwotche aneneli a Baal pa phiri la calimeli pa civo 29

Bambo atuwiri
8 years ago

Kulakwaa, Mulungu amapembezedwa ndi aliyense. Nkhuni zachita expire zulo pa Linthipe. Yalakwa basi Sailesi akachita blanda pa 37 minutes 19 seconds chigoli choyamba cha noma. 11 minutes 51 seconds gole wa BB AKASIYA Mpira ukulowa kumakawona ngati ukupita kunja. Chigoli china chikagola pa 91 minutes 36 seconds wogoletsa Fischer. Mpira ukatha pa 94 minutes. MANOMA 2-BB 1. MUsakachose coach akutelo ndi ambuye kuti zichitikedi zija zoti sibwino kusakaniza ambuye ndi satana.

Bambo atuwiri
8 years ago

Mene zikuwonekela game yapakamwa BB YAWINA 4-0 Koma 90 minutes yakuLILONGWE will make The NOMADS which people believe is not the people’s team be VICTORS of the day. By 5 koloko madzulo, Lilongwe isokonekela ndi 2-1 victory in favor of NYERERE

benidicto
benidicto
8 years ago

BB woyeeeee manona tiwaphunzise mpira.BB forever

UNECA
8 years ago

Apa ma fainals akoma asati akadafika matimu opanda masapotawa pa malawi pano ndi noma ndi bb wina sangakane.

AM CHATULUKA
AM CHATULUKA
8 years ago

Wamkulu ndi wamkulu basi. Chenjera neba, maule woyeee!!!!!

Concerned citizen
Concerned citizen
8 years ago

From failures to warriors,from zero to heroes,from nothing to something and from beasts to bests! Thats the spirit of NOMADS. We will make IT! Keep fire burning NYERERE ZOLUSA.

stevie njolomole
stevie njolomole
8 years ago

Ayi zabwino zonse. Ine maliro anga adzaika ndi aBB basi. Anoma ndichizolowezi chawo chomangoti tiwina. Bb ngati ingagonje kungoti yakwiya ndimizimu, chifukwa china ndi china bb ilbwino.

Read previous post:
Manganya brands ‘Satanists’ rumour mongers on Izeki

Comedian Micheal Usi known by his stage name as Manganya has branded people spreading rumours that skit star John Nyanga...

Close