Email a copy of 'Bullets plans to sign 6 players, Nswazi tipped for head coach role' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

32 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Mdicai Longwe
Mdicai Longwe
9 years ago

Izi ndiye zosamveka. Kananji mwadziwa liti kuti sakuchita qualify? Mpira simapepala koma luso la munthu. Team yawina Carsberg komanso league mphunzitsi wake yemweyi mukumunyozayu. Pano mukufuna wina wamapepala ake. Munali kuti nthawi imene teamuyi imavutika zakA TEN ZAPITAZO KUTI itenge chikho?

Pezani pena ponamira. Kananji yemweyo mothandizani ndi Ramadani apitirize kuphunzitsa teamyi. Posachedwapa Kananji munatumiza kunja ndi U17 kaya titi U23 simumadziwa kuti alibe zomuyenereza? Nanunso kuti tikufufuzeni ndi mpira olo omanga omwe simunasewerepo koma mukuyendetsa bwanji nkhani ya mpira?

ZONAMIZA ANTHU APA AYI!!!!

kumbukani Don Taulo
9 years ago

Carry on

Hassan
9 years ago

Zabwino zonse BB.

innocent
9 years ago

KODI MUNTHU MMODZI NDI AMENE AKUYENDETSA BULLETS ? KODI KAPENA NDI MSUNGAMA BULLETS ? AAAAA EXECUTIVE YA BULLETS VERY SLEEPING WHY ALLOWING ONE MAN TO CONTROL EVERYTHING AND NOW AKULANKHULA NGATI GS WA TEAM NDI IYEYO . DZUKANI DZUKANI EXECUTIVE ,SUPPORTERS ,TRUSTEES MUSABETSE TEAMYI KWA MSUNGAMA MBAVA . NDI MAFIA AMASEMERA ANZAKE ZINYAUTU AMENEYO. ANAMUSEMERA OPHMALLY KONDOWE NTHAWI YA BAKILI BULLETS .

Judge Kamisah
Judge Kamisah
9 years ago

Good plans BB KEEP IT UP.

Israel Difense Force
Israel Difense Force
9 years ago

Kodi all these dreams ndalama zake zopemphetsa zomwezi kapena mukapempha ku NAC???????

Koma Kondi Msungama has to slow down otherwise sizikulowera kwabwino ndi2, You are over dreaming ndithu sizikutengerani patali

Happening boy
Happening boy
9 years ago

I am 100percent nomad but i am really proud of a malawian club making such strides, i Just need to ask the club officials not call money into your bank accounts. Be prudent to mâle us more proud.

chaona
chaona
9 years ago

At one stage, prepare to face ama zambian boys. mad @ player ka bola.

James chilembwe
9 years ago

Bullets is gonna make it.

King salijen
King salijen
9 years ago

All de best

Read previous post:
Lawyer Ambokire Salimu in wife battering saga

Blantyre-based flamboyant lawyer Ambokire Salimu was on Christmas Day picked by Police after he  allegedly savagely beat up his second wife...

Close