Email a copy of 'Bullets players demand Lipipa, Mandiza, Gondwe and Malinga to resign' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

13 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
peter robert ngwira3
peter robert ngwira3
8 years ago

za ana a ma tiles!! palibe chifukwa choti apangile resign, munthu amakondedwa pa zabwino zokhazokha?? he is not God, & to error thats being a human………

SOLOMON MPETA
SOLOMON MPETA
8 years ago

EVEN IF THEY STEP DOWN WRIGHT NOW,AMENEWA AMAFNA AZIBA NDALAMA.

Tonde wa tonde
Tonde wa tonde
8 years ago

Why do u want Lipipa to resign ?mwadya ndalama zake ma player now u say he has to resign

Achiphwisi
Achiphwisi
8 years ago

Mbutuma zonse zosokoneza tadzichotsa..neba umawona ngati tidzingokangana woooo walephera

watipaso
watipaso
8 years ago

Vuto la ndudu kkkkk musova

gurugunya
gurugunya
8 years ago

Zayambikatu neba. Tiyenazo. Ndalama ndi satana. Munthu umatha kukana ngakhale m’bale wako chifukwa chakhobiri.

Nyatwa
Nyatwa
8 years ago

Mwapeza sponsor zalakwika, bwanji mukungokokanakokana mwawonetselatu umbuli

Mapwevupwevu
Mapwevupwevu
8 years ago

A Noel Lipipa chuma cha satanic chinatha pano akudalira khobwe ma ku Bullets basi! Ma Range Rover aja kulibe, nyumba zija anagulitsa molira kwa Rashy Gaffar kuopa kulanditsa, shame!

Achoke!

CHINGAMBWE
CHINGAMBWE
8 years ago

Iwe neba wayamba misala . Mmesa anthuwa unawasankha wekha pa masankho ? Lero aipa chifukwa akudzudzula a chilunga ochitidwa appoint , koma umphawi zoona sizinthu .

Ophiri
Ophiri
8 years ago

Fodyayooo! Fodyayooo! Koma ziliko kwa aneba.

Read previous post:
Malawi situation, living our faith …

Malawi is a country in Southern Africa. Malawi is infamous for its shocking levels of poverty among citizens. With an...

Close