Email a copy of 'Bullets players on training boycott, demanding signing on fees' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Bullets players on training boycott, demanding signing on fees' to a friend
An announcer at private Zodiak Broadcasting Service, Joe Mwase, and his secret married lover, Rita Chaima, spent last night at...
join clubs like BE FOREWARD, SILVER, CIVO, ndizimenezotu, rent akuthamangitsani. ndalama za SPONSOR zija adya zonse osakumbuka othamgitsa chikopanu? hedeee!
nanga bullets inayamba yachitapo chilungamo chiyambire? mbava zokha zokha. akamathamangitsana mudzingodziwa kuti wina akulephera kuba kumeneko. Siizo kunali Kondi! Kondi! Kondi! nanga lero ziri pati? ma Sponsor aja mumachita kuimira pa chulu aja akuti bwanji? anakupatsani, ndiye mwazidyanso? nanunso ma players kumalowa ma team ngati BE FORWARD, SILVER, CIVO ma club a chizungu, a atsogoleri opita ku church, not these bweka bweka BB
One million and demanding 4million
NAWONSO A STONE WO NGAKUBA
Always squabbles with this team why
Sad development that will not help the team no wonder the performance is not good. Please resolve the players issues as soon as possible. Nobody works well when he is not getting what is working for. This is one of the reason why football is not developing in Malawi.