Email a copy of 'Bullets says Burundian coach Ramadhan quizzed by Malawi Immigration department' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

18 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
good
good
8 years ago

Let him renew his stay. In a way this coach has assisted one of the best teams in the land. Be forward ingomeyani mpira osati kuberekedwa ndi makomentetazi a MBC nthawi Achinye Nkutu .

Paul Tyme
8 years ago

No more discussons just deport him.Why maforena amakuwonerera kwathu kuno koma kwawo amtithamangitsa ngati agalu?

chenda
chenda
8 years ago

Koma nde kumalawi lamulo ndilpweka,ayiwala zoti anawononga ndalama zambiri kukatenga anthu opanda zowayenereza ku jubeki. Chifukwa chani ife tikunyengelela ma foregners pamene amalawi akusowa mtendere kumayiko ena? Zachisoni kwambiri

Alex Grey Ndaipa
8 years ago

Chili kwa mnzako umati chigwire mnyanga, lungalunga mkubadwa, iyi sinkhani yoikoka ayi, chabwino kaya zimvere mtolo.

Mapiri
Mapiri
8 years ago

I have said this before and I will say it again, this country does not have good leaders. How do u allow someone to live illegally. He shud hav beem deported a long time ago. Go to RSA. If your permit has expired and you are arrested there’s nothing like negotiation. You will be deported. That’s why a Malawi is has a lot of illegal immigrants from everywhere. Can minister Atupele Muluzi and Immigration start working. You are sleeping on the job!

Yusuf Hofmally
Yusuf Hofmally
8 years ago

Tinamudziwitsa kale kuti pa Nyasalande lamulo silimagwila ntchito. Usaope ada this is law-less-land. Utha kumadya nzimbe ntaunimu sakugwila ngati muja amapangila pa Kigali kapena Bottswana. Utha kumenya mMalawi aliyesense, apolisi akakhala kumbuyo kwa iwe.
Utha kutitukwana anthu adzasekelera nanena kuti ndiwe wanthabwala!!!!!Permitiyo utha kumangowauza kuti uli busy upita ku Immigration ukakhala free.

Sydo
Sydo
8 years ago

Asowe

Lord Denning Chatsika
Lord Denning Chatsika
8 years ago

Sounds funny they say he was not arrested but he is on bail!

Professor Seyani
Professor Seyani
8 years ago

Seems ku Immigration ko kuli a Bullets ambiri. A Scova muliko?

PATRICK MAKWACHA
PATRICK MAKWACHA
8 years ago

MALAMULO A KU NYASALAND AMAKOMERA ANTHU OBWERA KOMA AKATI KUZUZANA TOKHATOKHA NDE NAMBALA ONE DZIKO LINO MUNDIFUNSE SILIDZALEMERA OSAUKA ADZINGOSAUKILABE OLEMERA NDIKUMANGOLEMERERABE

Read previous post:
Malawi gospel singer King James Phiri sued – Zodaik reports

Gospel musician King James Phiri has been sued for allegedly pocketing money for a show he did not perform. Civil...

Close