Email a copy of 'Bullets supporters committee top officials suspended' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

17 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Hd
Hd
8 years ago

Vuto la kumalawi la mpira ndi ku fam komanso ku sulom anthu awa akulephera ntchito yawo a daud nawonso ndiye kaya timaona ngati ali ndi masomphenya koma uuuu phala leni leni abotoman iiii ndiye madeya, madeya akenso mpunga akunja aja, water zampira za mkanika bolanso ntchito wayamba pano ija ndi winiko ya uneneri wa mpingo koma mpira nde ayi amalemba kochi oti angokhala mutu mulibe chilichonse ndiye tiyembekezere zabwino chimavuta nchiyani kupanga hire ma cashier amabank mu kuzolowera kuba basi muziva chifundo kungokhala anthu ouma mtima ngati jb ndi lutepo kufuna anzanu adzivutika nthawi zonse

Che Wanimiliyoni
Che Wanimiliyoni
8 years ago

Am a Bullets fan but sometimes this big club let me down in their thinking. I dont know whether its “..flash yanyimbo kale syndrome..” 1stly Joka investiments never pre-sold the tickets so how come they r being singled out when the gates were severally manned by Govt, Sulom and Police? 2ndly the players training boycot is out of order because as employees of the club they’ll get their monies regardless of whether the monies were stolen or not. I suspect somebody who doesnt wish Bullets is ochestrating this and my advice to players is to stick and die for their… Read more »

yakobo
yakobo
8 years ago

Vuto ndi Blantyre supporters amafuna kudyela team mmalo moyithandiza

cia america
cia america
8 years ago

awiriwa ndi amene anali potsogolo kti fote ndi kondi ndi mbavaa osaziwa kti mbavaa anali these two,the so called chibambo and tabwali,ndiye ku bullets kwanuku wabwino ndindani,basi i tink nonse ndi mbavaa including u the so called sapotazi

Chingolopiyo
Chingolopiyo
8 years ago

From local clubs {supporters and main exuctive commitees} to FA’s up to FIFA, the whole system is corrupt! Ku Bullets ndiye worse, this is why football can not improve

Alex Tulamah Tulamah
8 years ago

Onse acommet mitu yao sigwira muibela bwanji team yoti ilibe podalira osazimvera chisoni NEBBA mwana wako wakupwetekatu apa.ai ndithu pa MaLAWI pakuti waya mbitsa sindinu wayambitsa ndi MUTHARIKA kubela Dziko losauka kale Mmmmmmmmmmmmmm NEBBA wanga pepa

LIZULU
LIZULU
8 years ago

Inu a supporters committee mutisamale zomadyera timu tidzabwera komko ku blantyreko muwasiye ma player ndalama zawo ndi zomwezo alibe sponsor inu simusewera mpira ngati simungakhale mu komiti osasolora mutiuze ife tikhalapo ulere pampandopo bola timu ikamawina ife kumwa wa mkaka kukhosi mbee!!!

apm
apm
8 years ago

Ma game a bullets azikamenyera Ku Lilongwe basi. Kublantyre kwachuluka mbava. How can the teammake more money in mzuzu than in Blantyre? Stupid executive. Zakukanikani just surrender n leave our club alone.

Blessings Kaweru
Blessings Kaweru
8 years ago

Let’s be honest please it can’t happen big game to raise 16 million

KAMBWE
8 years ago

Mabvuto chiwambo ndiwakuba heavy…ndipo chomwe anabwelera amafuna kubako basi

Read previous post:
Misa Malawi censures Mutharika for attack on media: Repressive tactics unacceptable

Media Institute of Southern Africa (Namisa) Malawi chapter has advised President Peter Mutharika to refrain from attacking journalists and local...

Close