Email a copy of 'Bullets survive Dedza scare as Eagles, Mafco register wins: Malawi TNM Super League' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

11 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
William Tembo
William Tembo
8 years ago

League tatenga kale basi ife mapale.

khantitiwa
khantitiwa
8 years ago

Wankaka mpaka nselu retaining the championship

Hardson
8 years ago

Sorry ma bankers kodi zikukhala bwanji kumeneko. I have got prenty of strikers friends.

nyenyezi
nyenyezi
8 years ago

Nyasa Big Bullets to be crowned champions again? koma wina azimangirira akulu akale anati kuthyola khobwe ndi m’mawa anyamata a Nyasa Bullets anaumvetsa mwambiwu ndipo anachita zotheka kuti 1st round asagonje pofuna kuzichepetsera ntchito mu 2nd round pano palibenso amene angawapeze gap yonseyi, mwina mungokambirana ndi a SULOM ndi TNM kuti ngati khotheka matimu angapo asonkherane mapoints kuti aipeze Nyasa BB, apo bii, MK15m ikununkhira basi anyamata asangalale atagwira ntchito yotamandika mu bwalo la masewera kwina masapota osatekeseka tikumva kukoma kumwa wamkaka, neba akumwa wa mandimu koma ziliko liko ku Nyasa Bullets

AKIJA
AKIJA
8 years ago

apa zatheka kale ma pale

musova
musova
8 years ago

Bullets league yatenga apa palibenso angawafikire

wa bullet
wa bullet
8 years ago

The big team in malawi

Murray
Murray
8 years ago

Pang’ono ndi pang’ono mtunda ukutha……..

nyasa reporter
nyasa reporter
8 years ago

Mapalestina zikutheka

Paul Omaliza Makoka
Paul Omaliza Makoka
8 years ago

It was a good game koma Ref amaimbirayo mimba yake ndithu. Samadziwa chomwe akupanga mground. No wonder ndamva kuti he is one from Ayaya FC family

Read previous post:
Chisomo Machero is new Miss Blantyre: Malawi Poly student

Chisomo Machero, a student from the Malawi Polytechnic, is the new beauty queen for Blantyre city. The 21-year-old, currently in...

Close