Email a copy of 'Bullets to play two Mozambique clubs for Caf preps' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

20 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Komanso
Komanso
9 years ago

haahahahhahaha kodi BB izisewera CAF yokha? Kapena ma player amatimu ena mukufunawo azisewerera BB ku CAF kokha? ngati a BB mukufuna kugula player tsatani ndondomeko yabwino, timu ngati sikugulitsa player basi ndi wawo asiyeni. Ngakhale ku Europe matimu amakaniza ma player kupita ku club ina pa zifukwa kkkkkkkk

Amon Maligiya
9 years ago

ikanakhala mbuzi tikanaidula makutu kuti mwina ingayambe kuva amalawi tidzanva liti kuti nsanje siipindula yakwana nthawi yoti amalawi tisinthe ndichifukwa chake timapangirana nsanje ngakhale kudziko laeni

Kanthunkhaku Homeboy
9 years ago

Eeshhiiiii

chirimba boy
9 years ago

lets pry ziyende bullets ndi timu yadzikolonse anthu onse akuyebekezera bullets mu caf tiyeni tigwirane manja amalawi ndizanthuzomwe izi

brown
brown
9 years ago

Kuchulusa zoyakhura a bb mbuzi kkkkkk

Augustine Shaba
9 years ago

Gooo maule azachita manyazi

dickson jailos
9 years ago

Amalawi yakula ndi nsanje mmalo moti mulimbiki now ur still to useless even a bb wo atawina mukundiuza kuti that money zingapite ku zambia asi

alukosyo
alukosyo
9 years ago

Msungama and Fote involve your friends. zinthu sizikuyenda coz your attitude yozikonda

atate
atate
9 years ago

Matama achulukitsa a BB

Yankees
9 years ago

Mr Fote, where were U when Wanderes and Big Bullets sighned a memorundum of not poaching prayers from one another? Were U in Burundi or Algeria, can u say akutikaniza ma Prayer chonsecho u want those other clubs to die completely? Ife timati mwina mudzipempha matimuwo timafunako wakata wakati kodi kunoko tingasinthane ndindani? Munalowa Musanankhozeke? Then just withdraw matransfer akuoneka ngati anvuta awa? Mkazi ngati wakukana a Fote timakayang’ana wina!!! Dont forse a Horse to drink water men!!?.

Read previous post:
Malawi players Kawonga, Kachimanga in Mozambique for trials

Two Malawian players who play for former Super League club champions Silver Strikers left the country on Tuesday to Mozambique...

Close