Email a copy of 'Bullets win appeal, to face Silver at Mulanje Park in Airtel Top 8 second leg' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

7 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Kalulungusese
Kalulungusese
6 years ago

Good decision by FAM, hope Silver ikatelela kwambiri pa Mulanje than pa Zomba

Latson
6 years ago

I know that u are going to make us happy,sitikudya bwino ife ndi neba zake zikumuyendera,Make it happen ndipo zikuyambira pa Mulanje …Wamkaka tikuyamba bax wina afune asafune ….Ndilikomweko

pathfinder
pathfinder
6 years ago

Achimbalanga achitsiru inu. farm sikondera bullets koma apa yatsatila lamulo, ngati manyi akukolera pita ukanyere oko. silver ili ndi ground lawo koma inatsankha kukamenyera pa BNS, ndipo farm inaamvera polemekeza lamulo la ma sponsor, kuti home team ili ndi mwayi osankha ground lomwe akufuna. BULLETS WOOOOOOOOOYEEEEEEEEE KU MULANJE KOMWEKO KU SAPITWA. ma bankers akaone chimdima.

ONOMUNA CHIMBALANGA
ONOMUNA CHIMBALANGA
6 years ago

kodi a FAM mumakondera BULLETS CHIFUKWA CHIYANI CHILI CHOSE CHIMENE AMANENA INU MUMAVOMELA KALULU AMAFERA KUMODZI MCHTSAMBA

yazula
yazula
6 years ago

My beloved team Nyasa Big Bullets,please guys try your best to put a smile on our faces(MAPALESTINA) i wish you all the best as you go to Mulanje,i know u will make it PLEASE!PLEASE!PLEASE! Always on your behind guy,Mpalestina weni weni ine Maule for life!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!Goooooooooooal! Mussa Manyenjeeeee!Bullets 3,Silver Strikers 0,mpira unachoka kumanja kwa Dalitso Sailesi kudzagwa pa chipumi pa Mussa Manyenje nthawi imodzi,kusumbira mu ukonde chigoli mbambande………HAHAHA! Odi uko Maule ndinyamule basi cant wait.

ndondwa
ndondwa
6 years ago

Chitimu, once maule owz maule asafuna asiye iya

kings
kings
6 years ago

Thumbs to Fam official for sticking to the rules & regulations of the competition. For Bullets make sure ur appeal bear the fruits otherwise supporters won’t spear you once the game goes other way round.

Read previous post:
Malawi paired with Tanzania, Mauritius and Angola in 2017 Cosafa Cup

It's fair to say Football Assocviation of Malawi (FAM) is delighted with the  2017 Cosafa Castle Cup draw conducted on Tuesday  as Malawi senior...

Close