BWB auditor caught having sex at Mwaiwathu car park

A honry Blantyre Water Board (BWB) auditor and a woman have been arrested after being caught having sex in a Mwaiwathu Hospital car park, police have confirmed.

Sex in the car

Sex in the car

The 26-year-old internal auditor, Thokozani Maluwa and 20-year-old woman, Emma Peter were caught by a night shift guard while ‘in the act’ in a Nissan Tida registration BU 2489 parked at Mwaiwathu Private Hospital’s car park.

Blantyre police Public Relations Officer, Elizabeth Divala said the two have been charged with Idle and Disorderly under Section 180 of the Penal Code.

”They are still in custody. The guard caught them in the wee hours of today (Monday 16 March, 2015),” said Divala.

Maluwa and Peter told law-enforcers, during interrogation, they found the hospital’s car park idea for ‘car sex’.

It is not yet known if the two who are residents of populous Ndirande Township are in relationship or it was just a one night stand.

Maluwa hails from Sani village T/A Nanseta, Thyolo and Peter hails from Likoswe village in Chiradzulu.

Follow and Subscribe Nyasa TV :

Please share this Article if you like Email This Post Email This Post

More From Nyasatimes

More From the World

289 thoughts on “BWB auditor caught having sex at Mwaiwathu car park”

 1. FFFFFRDA says:

  inuso mukanagoti ndipangenawo basi mpaka ku polisi

 2. Chibankhuni says:

  Very chisoni,kumaganiza ngati anthu akuluakulu,zinthu kumagwilitsa pamalo oyenelera.

 3. Manzy says:

  Kwatsala kanthawi pang’ono kuti malemba akwaniitsidwe ndipo kuti mwana wa munthu awonekere ndi kutsika ku thambo

 4. Fraka says:

  Inde papsya tong’ola bro

 5. Man og God says:

  Ambiri tukulephera kugwilitsa ntchito bwino zunthuzi,ndipo zikuoneka ngati zoyipa papemene mwini chilengedwe anakonza kuti zidzichitika mwadongosolo komanso moyenela kwa anthu ovomelezeka kutero,zachisoni,zamanyazi indeed i agree,signs of the end!
  God can not tell or comand us to do a thing we are not able to do.it is possible to excersise self control! Works of the devil.Enanunso mukupanga koma simunagwidwe,chenjezo nali’mutsalatu mukapanda kulapa ndi kusiya uchimo cause Jesus is indeed coming soon,He is on the door! Samalani!

 6. Jagha-Yagha says:

  kukonda kumwa Yogh anthu akulu-akulu vuto lake ndilimenelo, kuthamanga magazi yimeneyi tingoti sexgate

 7. Trueworths says:

  Very shameful

 8. Thandie says:

  Signs of de end

 9. Maxwell says:

  Comment. Zovetsa chisoni

 10. mbaleya says:

  Thats forensic auditing in the car. economic by saving money for rooms. But i dont understand the case of idle? these peoples lower part of their bodies were moving( nyekhunyekhu)and not idol, disoderly maybe

 11. pk cream says:

  Guys
  Without Jesus u can do any sin, allow Jesus to be your friend.
  olokuyalukako azanu akulira mo hospital mo ndimatenda inu Muli busy kupasana matendawo shame on you.

 12. mike says:

  Kuufila

 13. chatonda says:

  Who has not sinned before to start condemning the two people above?

 14. big man wamkulu says:

  thyolo, mulanje, chradzulu…need i say more?

 15. PANALINSO ZA CHISHANGO APA ??

  MALE WATENGA ZOTENGA TENGA

  NKONA ACHINYAMATA AMBIRI AKUPULULUKA KAMBA KOPUPULUMA POCHITA ZINTHU

  NKHALAMBA ZILI PHEEE NDI MA KHISI A KU UKALAMBA PA VALANTINE

 16. Peter says:

  so pathetic a scene. The two people are young and that tells how immoral the future of Malawi will be

 17. Peter says:

  so pathetic a scene. The two people are young and that tells how immoral the future of Malawi wg5will be

 18. gondwe says:

  The Big Question is: Why God made this sweet thing? …………….Yes to use it……….so any problem as …….where and …….when and with…….. whom……and how…for…long…

 19. proud parent says:

  Filthy comments are a sign of the times. Before the end comes sin will multiply. The days are evil. Sin is a right. Aliyense agwiritse cimene alinaco Ambuye asala pangono kudzaweluuza.

 20. joseph makuya says:

  Nanga ku BWB kuli wogwira ntchito achi rasta? mungofuna kumiyipitsila mbiri mzanu agalu inu. Inuyonso ndiamene muli pa number one kuchinda ma hule.

 21. gondwe says:

  Mkazi uyu NDIWOKONGOLA ZEDI. EEEEEEEEEhhhhhhhhh enanu mnsanje basi. Mumusiye amuchinde zedi.

 22. Mac Javis Andrew says:

  Koma zina zimanyanya mpaka kuchipatala? A-aaaah sanalakwitse kuwatsekera ku Police kuti ena atengelepo phunziro. Komanso zangoonetsa kuti abambowa ndi nchitidwe wawo. Komanso akaziwo ndi a Hule. Salabadila za malo ochitila zogonana.

 23. Giffy says:

  Never seen a Green Nissan Tiida so far!!!

 24. prescott Tambuli says:

  Kh!k!k!k!k!KKKKKKKKK Mlondayo amasirira mkazi wokongolayo. What a shame! A whole Police officer wasting time pouncing on pairing individuals. Why is it that women are roaming our streets almost naked these days? What do they want? I thought they want to be served? Then don’t you know that denying someone sex is a sin? Why are you not arresting those robbers who are terrorising our locations? Mwasowa ntchito eti.

 25. zilipati? says:

  Asiyeni

 26. Wakukaya says:

  I don’t know why people become so interested with such issues when the truth is having sex nowadays is obvous. It doesnot matter the place where you are so long there is an agreement between a man and a woman. Anthu nsaje basi. Anzanu asamanve kukoma. Tangowatulusa pabelo basi. Aliyense amapanga zimenezo, aasssh. I think the guard overheard the screaming of the two!!!!!!!!!!!!!!!!! kkkkkkkk. Kaya?

 27. tsutsube says:

  Nonsenu muone kuti nkhaniyi ndiyabodza monga Nissan Tiida imaoneka chonchi komanso inu mukulimbikira pomwe mumapanga zomwezo ndipo zibwenzi zanu zangoti bwee ngati nthata za Galu okalamba .Musalimbane ndi kumangolankhula zammaluwa.

 28. omawe says:

  Kunama ku Chiradzulu kulibe akazi oyera chonchi.

 29. Allick Tembo says:

  Zimatero, Amafuna kutchuka. family yake amadziwa kuti wawoyo ndi otero.

 30. Mercy McLean says:

  Pali chani apa.. tapangapanga zimenezi.. bola osagwidwa.

 31. Auze says:

  Mmmm shame to you all

 32. Rhodriguez says:

  EEEeeeeh ma man phuma, mpaka mkati kati kati mwagalimoto. hehehehehehehe

 33. Magang`a says:

  Sex ndi Sex basi iye Mlonda chomwe adakachita ndikupempha kuti naye adye nawo basi!! Tandiuzani anthu nonsenu ndindani sanadyepo punani mma resthouse ali mbweeee mmakwalalamu???? Enanu ndiyetu mwachindana mpakana kujango!! ndiye za anzanu ndiye kuziika pambalambanda choncho????

 34. eye witness says:

  Ukayenda ndi Mulomwe wayenda wekhadi. Sheeeeee!!!! si Alomwe amenewa?

 35. chrisaukira says:

  Comment;Dogs.

 36. chimwemwe chimtengo says:

  Dziko lili kumapeto owerenga khala maso.Zamanyazi mwana wakwathu.

 37. ujeni says:

  Am finally forced to comment on this story and photo. This is not the actual photo of the malawians caught. This photo is foreign and has been put there just for illustration. Now i know why we have useless leadership in Parliament and government, we voters are cluless, ignorant, stupid and dull.

 38. Redeemed says:

  I wonder why women are always on the spotlight, I could hardly recognise the guy, but the woman’s identity is completely exposed. I wonder how his family will handle this shame.

 39. apanga bwanj zopangazo asanagwirizane? Ndekut anagwiriza kut apange zopangazo, nde palibe mulandu apa

 40. malawi says:

  koma adonawo nde inawafikapo ndithu kumuloka kumeneko? ma Judo moves hahahaha

 41. walakwisa chan munthu kudya zipaso zapakat pamunda? Aaaaah nsanje2 iyi apolice

 42. Che Smoko says:

  Kodi atumbuka olo a Chawa samakwata……… Nanji a Tumbuka kukonda kuzijambula, muti chani pano Anyapapi inu asa

 43. nyani ndi munthu says:

  size ya bwino,kuchinda siwaletsa!

 44. joe says:

  Comment. How could u possibly get a photo coz when the guard found them they must have covered themselves first mabodza a malawi

 45. NOVILIKANA says:

  mphuti na matongo kusangana kkkkkkk

 46. Hot Iron says:

  A Polisi komanso a Court, agendeni miyala anthuwa ngati simunachimwepo. Deal with mbava zikuvuta m’madelamu please. Atayeni achita manyazi okha dziko lawo lomwe. They have learned it a hard way – apeza polekela and a lesson to many across.

 47. kachindam'bwete says:

  Akwatana akwatana basi, inu simumachinda anyasatimes? Ngati amabzopelana mu galimoto yawo inu chakuwawani mcha? M’bwete kaya mbolo ndizawo, ndiye inu ndi asakwata kapena kuchuluka mzeru? Zapamtumbo ndithu

 48. Poga Wandale says:

  Whu really took the picture?

 49. Getrude says:

  Do not wonder brethren, it just signifies that Jesus second coming is nearing.

 50. bakayawo says:

  Mwati kunali ku chipatala eti?

 51. ine says:

  I don’t see the reason why you ppo shd publicise this … iwowa ndiwoyamba????? timamva nkhani zambori koma sizifika apa

 52. Chindazi says:

  The Internal Auditor was checking the internal Controls of Emma Peter….kkkkkkk but in the car why…… these pipo are not married…. Emma Peter should be a Prostitute…. Do you think a wife can accept in the car…. or ndi mkazi wamwini wake……..

  Koma mwayaluka,,,, nyere imeneyo……agalu eni eni….

 53. Nthawi zakumapeto zobisika zikuchitika poyera ngati nkhuku.

 54. Zanga Phee! says:

  Let it be, Mlonda something was wrong with him, how could he alarm on this simple issue perhaps he is looking for promotion,and again the whole process of inviting the reporters with their cameras on the shoulder coming closer to the sin it would have been too late to pic them a picture so it means Nyasa reporter they don’t sleep as well.Because they didn’t say Photo by who please tell us who took the photo at that time Alonda can’t have that powerful Camera. See my name

 55. nneka says:

  koma munthu amadya bwino uyu,mawa ndi iwe ndi uyo.

 56. Kukaya Wa Kukaya says:

  These are real signs of end times. Why accept to be used by the devil in this manner? Please repent of this act and seek the face of God immediately.

 57. kapambwe says:

  Let’s restrain from such embarrasment. Their are so many cheap rest houses in Blantyre and Ndirande in particular. One would have called for reservations at one of Paseli’s. The owner doesn’t steal cars he steal house tiles. His charges are within affordable standards. Please stop exposing the necesities unnecerily like this by pretending there are no hospitable places with no Bed bags. Kkkkk.

 58. Botsotso says:

  Tazimvera tokha kuti ndi mwana wa Peter pulezident

 59. lucky says:

  Amalawi, kumeneko wapolisi kusaziwa malamulo, mlandu wanenawo ndi ogwirana2 za malove ma public place pomwe dis two were caught red handed in de act, its lyk munthu wagwidwa ataba katundu nde ndikumamuimba mlandu ofuna kuba. Does it make sense. Penal code 168 re-ammits plz.

 60. tuliwuli says:

  Koma panavalidwa condom apa.

 61. chimidzi says:

  SO AMALAWI MUKUPUSITSTIKA KUTI THIS IS A REAL STORY JUST LOOK AT THE PICTURE
  THESE PEOPLE WERE MAKING AN ARMATURE PORN SHOOTING AND THEY ARE NOT MALAWIANS.AKWAAAA

 62. Nyapapi says:

  Basi enough! Stop making stupid comments and get back to work! Fools!

 63. zell says:

  reggae in the bathroom, reggae in the kitchen. …

 64. KRIT says:

  waulula chifukwa sanamulipire Mlondayo. all guards in twn lent out spaces, corridals to short time sex addicts

 65. kadome says:

  alonda muzigwira mbala osati anthu oswa tchende

 66. KRIT says:

  Its Good to let them go. it was a perfect hideout for them

 67. zweli says:

  ma rest house onsewa mpaka mgalimoto ndiye sanafilanatu zimafunika malo otakasuka izi………….

 68. One Loves says:

  Mwati mulondayi anali ndi Camera kapena this is just a sample picture of lovers having sex in a car?

 69. dezmond says:

  hahahaaja asiyeni mesaaa amaufilaaa

 70. himself says:

  Y getting them in custody * they jst expressed their feeling in they owncar * akulakwilani kalikose ngati

 71. tuvi says:

  koma eeeh wonsewo akuoneka kuti amanjoya , amamva bwino, ai apolisi amasuleni sanagwirire ayi this was consesual sex

 72. Mmmmmmmmmmmmm,nde ngati eni ake anangwilizana ungakhaleso mulandu?Atuluseni alibe mulandu ku boma koma kwa mulungu.

 73. pastor ernest wahiya man of God says:

  Naweee anena za alomwe apa

 74. sadick says:

  Koma anakasiya amalize kae asanagwire, koma mlonda chipongwe.. Lol

 75. che Mbela says:

  Charged with Idle and Disordery Kkkkk disorderly maybe but surely not idle Kkkkk

 76. dave says:

  Amene wakhala ndi galimoto for more than 2 years and lives in town…pali chachilendo apa??? Tithokoze sitinagwidwe and nthawi imene tinagwidwa tinalipira guard or s neighbourhood or police msanga and zambiri

 77. pastor ernest wahuiya man of God says:

  Comment: aaaa mukuwagwila anthu oterewa kusiya mbava ma office mu

 78. koma kumwera mwanyanya zochitika eeeeee ma lubino mukuwapha,mgalimoto kugonana, mavoti kubera, kodi mukutenga dzikoli ngati pa ground pochitira zopusa eti oooooo Lord have mercy on us

 79. Isaac chagwa mzuzu says:

  Sodom and Gomorrah

 80. mike bumbwe says:

  zowona mpaka kuvula zovala zonse mu galimoto

 81. bentby smart says:

  Alhomwe ndi choncho manyazi alibe. Ayesa mlakho woyendetsa asikana mawere pamtunda. Shameful

 82. Big Punisher says:

  Is this newsworthy?Two consenting adults at it during wee hours probably if it was during day time.Alendo amanyanya kuchuluka pa Malawi moti eni nyumba decided to leave their house to find a refuge in a car.When natures takes charge,U lose your mind sometimes.

 83. ahoy says:

  Is this the real picture. Doesn’t look like night

 84. Mduli says:

  if the two agreed whats wrong there?

 85. chiswabumbu says:

  Kuswa matongo no size

 86. Chatty Man says:

  Fifty Shades of grey!

 87. Elliam says:

  Mwikho yeeeeee

 88. precious says:

  Comment koma milandu inayi.

 89. Doctorsmh says:

  Even real Doctors Fuck Nurses when the Hospital is so Quiet and we Know it, OSANAMIZANA APA. Deceiving their wives kuti Patient wadwalika kwambiri and yet they know that the Hospital is so Quiet.We can even Name them right at Mwaiwathu Hospital. Doctors even SLEEPS with Patients there.

  1. dungulinya says:

   Atchule aise timve

 90. English Guru says:

  so nyasatimes, you only publish comments that do not criticise your editorial skills and/or adherence to rules and ethics that govern your profession. you hide behind “comment awaiting moderation” when in actual fact you are censoring comments that are not favourable to you! as far as i am concerned, your censorship should be aimed at filtering those comments that carry content that is objectionable for public consumption. we only criticise you if you go wrong because we want you to be the best, bring us well researched, well written materials, not stuff that does not make sense! grow up and stop running personal vendettas against certain critical commentators or just remove the option to comment altogether and just feed us your lies that no-one will question!

 91. henry ja says:

  Hahaha I don’t think its acrime.coz they were nat doing that at apublic view. Remember tha same act that happnd at the airport. Apriest and anun they were nat arreste,so police let it go, and concetrate on big crimes that r happnn in malawi everyday.

 92. Pitala Mathanyaula says:

  Koma Chilungamo apa, Chimkazi ichi ndichoneka bwino, sangapilire nacho or pamsika atha kungo menyapo basi. sheeeeee. Nothing wrong here.

 93. Greencardless Malawian says:

  Alomwe pa chigololo…..!!!!!!!!!!!!!!!!

 94. roots says:

  Let them go, kalimbanene ndi omwe akugulitsa mafupa awanthu wa!

 95. BigMan says:

  Please, let sleeping dogs lie.

 96. Arthur says:

  Yah in last days zobisika zonse zidzaululuka. I hop we are in last dayz…..

 97. Arthur says:

  Yah in last days zobisika zonse zidzaululuka. I hop we in last dayz…..

 98. mlaa says:

  Surely.

 99. Tatas says:

  Comment zadziko zimenezo

 100. vuto wato kamil says:

  amangidwe basi

 101. Rodriguas Latata says:

  Idle and disorderly? Is this being idle? May be disorderly but difinately not idle. Idle? Eeeh! Eeh! Eeh! Idle? No! No! No!

 102. Manyuchi says:

  Kodi a police kodi mesa mahule mukawagwila mumagona nawo kuti muwataye.Safuna kudya zabwino ndani?Guard iwe sudakumane nazo dikila Nachipanti akupeza kkkkkkkkk.Tamangani akubawa osati olongosola katundu umbeta utivuta apaaa!!

 103. baleke says:

  Too bad

 104. prosper says:

  total waste of state resources pursuing petty issues. police plz concentrate on real crime!

 105. hoveliwa says:

  Commentkupusa umenewu ndi mlandu amachotsa Mauka. Apolisi zomwezi?

 106. Kwaderatowi says:

  Angulu amenewo, atakhuta njoka.

 107. Matimati says:

  Shaaaaaah!!this’s not gud uwu ndi mwikhooo bwanji utchisi kuwasemphatu ur frendz kumeneku!

 108. inkata be says:

  But were the sister and. The father that were rocking a ca rat the airport arrested? Plse someone remind me.

 109. Tina says:

  Zakukomeranitu koma ma post a mau a Mulungu Ndiye no comment

 110. miss independent says:

  Kodi inu bwanji? tawasiyeni anzanu amamva kukoma …. nsanje bwanji?

 111. kanyika dk says:

  alomwe fakafaka muchulukane basi,nde ndi ma floods njala kaya

 112. imvani za ine says:

  Sex is a natural thing mukuwalengezeranji? If thy are having sex it fully means anagwirizana.

 113. Ophiri says:

  Amenewo ndiye alomweo

 114. Ophiri says:

  Alomwe omweo kuti wa wa wa!!!……singing

 115. social analyst says:

  those who say alomwe please dont remind us of the nkungula-msiska scandal?

 116. opportunist says:

  Kuphaka life .Tidye zimenezo. Kunja kuno kwabwera malungo

 117. collins says:

  Comment; we need faces.

 118. Comment munthu ameneyo kuvuta ndi kwake basi.

 119. puludzu chisale says:

  Kkkkk zochititsa manyazi

 120. shango says:

  Ziwanda zoipa kapena kufuna kutchuka aaaah

 121. lynoxm says:

  anaonjeza koma amaleka kupita Ku lodge bwanji komanso main a anagwirizana ndi mlondayo ndiye sanapatse ndalama yomwe anagwirizanayo.

 122. Nyepeliwa says:

  Zitsiru…auditor and u cant afford a room,u shud be fired frm ur job…galu mbuzi

 123. stefano says:

  Alomwe, eeeeeeessssshhhh

 124. inkata be says:

  But were the sister and. The father that were rocking a car the airport arrested? Plse someone remind me.

 125. weniweni says:

  Koma ofunikadi kuxamala coz izi ndizizindikiro zosonyeza kut dziko likutha bax coz zinthu zomwe zimapatsidwa ulemu pozichita nd kuchitikira pobixika nw zikuchitika pa mbalambanda ashiiiiiih so shameful.Comment

 126. Thitherward Wendo says:

  They may have found the hospital’s car-park ideal for car-sex, but I’m surprised that they found the Tiida ideal for it.

 127. mgawadere says:

  Alomwe mwaona

  1. Amunabawa says:

   Zugwirizana chani ndi alomwe
   Wachamba iwe ndikupeza

 128. ramsy says:

  Koma anaendacho chi MDIDI?apatsirana ebola amenewo anyenyeka maliseche asieni

 129. tito says:

  Sex knows no place and no time

 130. Ovilera says:

  In the last days……

 131. Kaidi says:

  Idle?….didn’t you say they were having sex?

 132. Kosmas says:

  Atengera ambuyawo a Chief Executive aku Blantyre Water Board Thawe amapanga muofesi ndi macleaner, secretary and internal audit manager

 133. otate says:

  The guard is stupid

 134. Mac William Shumba says:

  Amenewa zitsilu xa anthu kunalibe malo bwanji kunyumba muwamange zaka zambiri atengerepo phunziro

 135. anabel mitawa says:

  now I know why BWB can’t supply water to Bt

 136. eva says:

  Commentkkkkkkkjk koma nde chilimotu sungapilile.

  1. Charger cha mutu waung'ono says:

   Chachita kuvalira mkanda wa golide amwene

 137. Okhrana says:

  Onse akuti alomwe alomwe kukonda chigololo ndi agaru, alipo asamakonda chigololo apa? Achewa ndi atumbuka ndiye nkhuku zenizeni ngati munatulutsa porn ya ujayu timutchule mkadzi wa….. Ndiye awa ambeta vuto nchani zazii tapangapangapo ife parked pa njira

 138. brighton says:

  ZOPUSA

 139. Phuranya says:

  koma ya mpakana pamenepo

 140. Kokotowa says:

  What a true internal auditor! He was literally internal auditing the woman! Kikiki!

 141. Wezi chimubo says:

  Koma chisembwele at peak

 142. Nanseta says:

  mu galimoto? Car park ya kuchipatala?? Nyere zoopsyatu izi.

 143. Choster says:

  yamugalimoto mmene imakomera zangolakwa kuti awagwira koma nateso mpaka ku hosper!!!!!!

 144. Mangulenje says:

  This is not news…. not even a police case.

 145. Gringo says:

  Alomwe. Gondolositu ameneyo

 146. spanyola says:

  Koma anawadikira kuti amalize?

 147. Emma Peter Mutharika, mpaka mikanda m’galimoto? Uli boo.

 148. Nyapapi says:

  Kkkkkkk ndye idakugazula2 nyele, mpaka kufika pamenepa,,,, shaaaah…..

 149. Elton says:

  Ziwanda zikakhozokela mapeto ake ndi amenewa

 150. one love says:

  Comment kodi asanakwanitse marriage age? alawe basi!

 151. NKAWERA mrs says:

  auditing inavutatu pamenepa

 152. munthu says:

  Chigololo chilebe manyazi…pali ponse..ndiye kuti ziwalo zawo mzamoyo

 153. victor says:

  Commentkkkkk anakawadikila amalize naye mulonda osangoyipempha kuti naye apangekoso

 154. Amalawi kulakwa sikutengela mtundu inu mwaziyelesa koma Mulungu akukudziwani let’s condemn the action but not associeting it with any tribe.I love u fellow Malawians

 155. chris says:

  Comment mulungu akuchedwa kubwera anthu mpaka kumayaluka chonchi iyi nde nthawi yeniyeni ya sodomu ndi gomola

 156. mdf says:

  Sex ilibe malo….pali ponse zitha kuchitika bola ngat pali quit

  1. CHEMMBALUKU says:

   very right buddy. anthu akumapanga even muma Casper, cruiser, kuseri kwa club…… sibola asawapeze ……its cats sleep anywhere… in the casper…..by the club……koma kumeneko…..kkkkk

 157. Munyalapa says:

  Ma feel basi, kape ndi guardiyo. Chisembwele sichiona mtundu.

 158. zilimmalunje says:

  Alomwe uhule

 159. wanted says:

  What is strange here

 160. edda mwalweni says:

  Abale, mpaka kuchita mgalimoto? Munaganiza banjo pamenepa?

 161. mphwanye says:

  alomwe zili ndi eni ake izi. Midyomba, a tonga angoni ndiye mashasha. mwawona inu mwati muyesele akupezelerani. ahlapwa!

 162. chitengo says:

  Kodi agalu achisika amenewa ndi apabanja? simunanepotuapa

 163. Quingu says:

  Amalawi tisataye chikhalidwe chathu.tizisiyanese ndi zinyama mpaka mgalimoto kuchipatala shame

 164. Micdad Msosa says:

  Zamanyazi mpaka pamenepa?

 165. onjoya says:

  Kodi vuto ndi chani

 166. jimmy ka says:

  This must be the end of ages.

 167. herbert says:

  Mulungu akawalanga ngati salapa

 168. Munthu aliyense ali ndi mistake imene anapanga kapena akupanga kapenanso adzapange pepani abale

 169. condom says:

  kumakoma nthuni!!

 170. Achimidzimidzi says:

  Watchman is wrong he could have asked for his turn.
  Pakabwadwa mwana dzina lake akhala Hospital

  Ndilande ikusungira ma actors a BM eti.

 171. steve says:

  mlondawatulo osangopenpha cash kuauzakut pangan mawa mubweleso,mzafaosauka

 172. Ding Dong says:

  Alomwe Alomweeeee!!!

 173. chaiwone wawo says:

  Bola awa . At least they are not catholic brother and sister at the airport.

 174. Mngoni says:

  Alomwe kukungulana at its best, chipatso cha pakati sikukoma kwake.
  Nchifukwa chake mabanja sakulimba azimayi ndi azibambo kulowetsana kwambiri, paliponse tchende lilowe basi zomvetsa chisoni!

 175. enyana says:

  Osamangoti alomwe chilichose ,kodi simukumudziwa NYACHUSA wa ku Chitipayu. Wangobisa dzina lake mkumati Emma Peter.

 176. Anda says:

  Koma iyiyi ndiye yachabe tu.. Ma guy muli Ndi skill. Kuzipinda mu Tiida, Ngini kulowa ndikumamva tswetswetswe choncho. Iwe di Ndi auditor mapeto…. Team alomwe basi…hehe

 177. Amakoma kapena mwamvaana bwanji? Alonda bwanji osapemphako iyayi.

 178. Maliseche aAPM says:

  Alomwe zomwe amadziwa ndi zimenezo. Kuphwando la mulakho amangokhalira zomwezo.

  Pitala wachita kudzitsekera Ku nyumba yaboma, kutandala pa mwamba pa Gertu. Malemu Bingu kuti azimwalira nkhani yake ndiyomweyo.

  Mpinganjira sankati walanda liti mkazi wamwini. Mtundu wa anthu okonda komwe anachokera ndipovsindinaone.

  That is why they will always steal government money to have all women for their insatiable sexual appetite.

 179. Namonde says:

  Koma Mkaziyo Amapanga Magonedwe Amenewo?

 180. Payelepayele says:

  Alomwefe ndi deal,,,,,,,,,,alomwe woyeeeeeeee! Inu mmaona ngati ma boobs timashainisa aja ntchito yake ndi chani?????? Get over it,,,,,,,am proud to be a lomwe

 181. wanda says:

  Abale , atsikana achilomwe kukoma zedi. Amaitha ntchito imeneyi ndi chifukwa chake suona malo ogonana. Tawalaweni, muzavomeleza. Kkkkkkk

 182. Masambero says:

  koma the issue is Mulonda angakhale ndi fon yoti kudyambula foto ya quality ngati imeneyi??? Nyasaaaa mwatinamizatu apa

 183. akulu says:

  Wangochita tsoka Ku Blantyre azilonda ama parking a ntauni amachita kucharger anthu kuti adzipangilamo zimenezo.

 184. muhamad emwazi says:

  Kaya masiku ano azimai powakwata akumakonda kunamizila kulira kaya ndizemene mukuuzana mma kitchen top up kaya? Mkaziyu ati amalilira zedi mpaka kumamveka panja

 185. Nthalire Boy says:

  Watchman anasilira koopsya weee hours

 186. Wesley Milanzi says:

  Comment Yeah thats their business let them be more over it was night.

 187. cjp. says:

  Koma nde fucking enienidi. Ndiye anayilotsa mkatikatiiiiiiiiiii,,,, eshiiiiiiiiiiiii,

 188. Wesley Milanzi says:

  Comment I think thats their business.

 189. benjamin h. good says:

  Hahahahahaha akanangobweraso ambuye yesu wins azatifereso basi, kodi umunthu wanthu uja uli kuti? Tikuziyalusiranji anthufe

 190. Tsamba Likagwa says:

  Yemwe sanachimwepo ayambe kugenda anthu awiriwa.

 191. Bwampini wa Muthanyura says:

  Yes, the impact of selebwede cultural dance. Nde mwati ndi a mpingo wanji?

 192. Kadakwiza says:

  Alomwe ndi choncho. Musawadzudzule ndikhalidwe lawo. Ngakhale pa tchire amakhoza kupanga nkhani yimeneyi. Mulando umenewo chilango chake ndi zikoti basi mwina 12 zikoti kenaka azipita azikagwira ntchito. Palibe nkhani pamenepa. Ndizachi lomwe izi.

 193. junk says:

  for thoz that think this is the foto of the real act pepan kwambiri.. that shit is jst there for visual purpose and nissan tilda simaoneka choncho. stil more wat these pipo have done is moraly wrong

 194. Amene sanachitepo ayambe kuwagenda miyala

 195. Patriot says:

  Marriage bill igwire ntchito kikiki

 196. mbanga says:

  Koma ndiye kwa namseta

 197. Paul Dolezar says:

  Nawe Reverend Father Dasiano Muhime usamale udzagwidwa. Unachita zazikulu ndi ana aku primary ku Namulenga ndipo unali rapist.

 198. APM says:

  apa pakufunika graffiti, “thoko maluwa and emma peter were here”. kikikikiki

 199. James wa bakali says:

  kunyengana mpaka mugalimoto osakabuka room bwanji mbuzi za anthu zoona mpaka mbulanda

 200. Senior Ebola Wachiyao says:

  CommentMulomwe! mulomwe! Sazathekanso basi pa nkhani yosoka sokayi………..Mpaka kusoka ulisi wa white Ûtatha? Mbola.

 201. aledi nkata says:

  Dzana lija ndi ku airport.lero ndi pachipatala.HIV itha tikamatere?Taonani sadavalenso condom.KUPUSA

 202. Charger cha mutu waung'ono says:

  Sititengerana ku malo odula ndi babie yanga koma love yokhayo ayaaayaayaaayayayayayaua sitipatsana dollar ndi babie yanga koma love yokhayo ayayyayayayyaaya.Koma ndiye chimamunacho ndiye chikumukumba nayo mkazi,Taonani masowo wayiwaliratu kuti ali pa car park

 203. Khongoni Boy says:

  Alhomwe Kukonda Mbolo

 204. che mbwiye says:

  mwamva ndani kuti anthuwa ndi alomwe? mwaonera chani?

 205. dapalapa says:

  Dogs(agalu)!!!!
  However enafe mwina sitinagwidwe but this moral decay.

 206. knox says:

  Mathero adziko

 207. Steve Austin Stone Cold says:

  Alomwe mpakana pa car park marest house kunalibe mwachikondetsetsa motani chigololocho? moni kwa Pitala

 208. Wodya za NAC says:

  kodi angulu amenewa mmene amapita ku hospitalko anadutsa ma rest house angati?

  kukhwima basi? usawi, chi?

  Alomwe Kutha cooooooopy

 209. Damzy says:

  Kusowa ulemu,mbulanda chonchi?

 210. Zamanyazi kwambiri kusiya manyumba anu shame!

 211. joe says:

  note that this picture is not for Thoko and the woman so check your comments

 212. cash gate says:

  koma ndiye, mpaka mgalimoto, shame on you.

 213. mwandiyamba says:

  zitsiru

 214. George says:

  Very sad moment I think we are in the last days indeed let’s pray hard Malawians

 215. frank says:

  Alhomwe mbuzi za anthu m’paka chigololo m’galimoto mulibe wulemu inu, ndinu wopanda nzeru ngati pitala matanyula

 216. Pimbiton says:

  What d’you thnk mulhako wa alomwe is all about? Kup**lanatu basi!

 217. Bola akhale anamalizana chifukwa ngati anadomola asanakodzere awalakwira ayaluka uleletu.

 218. eliza says:

  Kma nyere zake nde zinafikapotu zosaganiza nazo zopita ku room kkkkkkk

 219. zanga phee says:

  Koma ameneyu, mpakana mkanda wa green mchiuno, ukumva bwanji mzanga wogwira ntchito ku BWB.
  Ma Rest house onsewa mwapwiya bwanji. wayalutsa BWB , kenako mudzapangira mmadzi.
  koma eeeeeeeeeeeeeeeeeeee chinakoma mpaka kuiwala kuti muli mgalimoto. satan anapondadi ndi mapazi pa Malawi pano.ukakhala iwe EMMA mmmmmmm,yalakwa,koma pamenepa Chishango chinatchenedwa apaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaa?Zamanyazi zadi.

 220. Emmatuwa says:

  Alomwe woyeeeeeeeeeeeeeeeeee

 221. bbsupporter says:

  GOD have mercy on our beloved MALAWI.

 222. nazimbiri says:

  londa siopusa,azilonda ambiri amaopyezedwa ndi zitsilu zimenezi.komwe ndimagwira ncthito,abwana athu amakhalira kutiopyeza kuti amatilipira,makamaka londa anatomuuza choncho tsiku lina

 223. jetro says:

  This picture is not related to this story. To those who owns or driven a Nissan Tiida you can agree with me that the door handles for this car are not for Nissan Tiida and so far I haven’t seen a metallic green Nissan Tiida. Bad morals though of having sex in the public and worst at a hospital car park. Shame indeed.

 224. Comrade.com says:

  Koma mwarinyu, mwari murima mbee!?
  Pali nkhani apa?
  Iwe Mlonda, kusavinidwa eti?
  Eeh, kwanu nkwani?
  Ukasuzumira iwe umafuna uone chani?
  Zizizidwa choncho anzako naatomuchinda nkazako iwe uli kogwira anthu ochindana.
  Ambiri masiku ano ndiyomweyotu.
  Uisova.
  Inu ku Policeko, amasuleni awiriwo azinka akapitirize basi.

 225. Anthu amenewa ndizitsilu eet kuitenga galimoto ngalimoto ngati nyumba mwaona momwe agwililanamo kuiwalatu kumeneto musawalange angotenga akwitilane chifukwa ayaluka kale ngati ali ndimabanja awo ndiyw kaya

 226. KUWILA CHILAMBO says:

  Ndi makape amenewa mpaka kubvulira zobvala sex ya mgalimoto. Shupiti!

 227. Nyapapi says:

  Alomwe ali ngati atumbuka, kukonda chigololo kwabasi!

  1. Kwame says:

   Pali atumbuka apa galu opusa ngati mako ndi bambo ako. Kudana ndi atumbuka bwanji anakudyela chiyani mbuzi iwe. Osakhuzumuka bwanji? Kambani za omwe amapanga chigololo pa malo olakwika osati kutchula mitundu.

 228. Marcus says:

  alomwe ndi khalidwe lawo alibe ulemu pa chisembwele

 229. MBACHI says:

  Comment MULI BWANJI ALOMWE NONSE KUMENEMULIKO? MUAPATSE MONI A PITALA.

 230. Mchindo.com says:

  Ine ndiye ndinapulumukatu coz mugalimoto ndiye I enjoy it osati masewera. Koma sindidzapanganso ndingadzayaluke eish!!!

 231. Hzwyzj Ian says:

  Mulonda wopusayo osadyapo za ku BWB unali mwayiwako m’bale pamenepa ukanakolola posafetsatu. Any time and place is Sex time and place as long as there’s nothing to disturb the action.

  1. proud parent says:

   I pity you.

 232. osman usu justin says:

  Alomwe alomwe nophuyaaaa,mpaka mgalimoto mwationjeza tu!

 233. Zayamba kuchitikira poyera eti? Kutha kwaziko ndikumeneko uchisilu cha umunthu basi kusiya mabanja kunyumba kuzagwidwa ndi hure kumeneko. Galu inu

 234. mbani says:

  Alomwe that’s why we were using NAC money

 235. Ngongoliwa says:

  A Malawi??? Mpakana kuchipatala abale? Ena adzakuchitiani inu zoipa kuposa apa

 236. Moffat says:

  Amangitseni woyera akondana… Too much hotels in blantyre eish!!! Dirty act

 237. midnight 6 says:

  Alomwe nde kukhala kwawo , nde muziti angalamulire chonchi? mbuzi za anthu izi

  1. benard riviel says:

   Iwe usagwiritse ntchito dzina la alomwe mopusa chifukwandikhoza kkuchotsa nkhwiko mofulumira zandiwawa.

 238. Ambulaje Ambulaje says:

  Akanayika poster: Internal Auditing in progress, keep away!!!!

 239. kenwizz says:

  Rubbish..please go catch and arrest these thieves that are terrorizing many homes in cities. Tikulephera sleeping in our homes because of fear and your wasting jail cells for this? The stupid guard was supposed to knock on the window and tell them to get off the premises. What is wrong with Malawi. This is so frustrating.

 240. JACOBS says:

  CommentALOMWE!!!!!!!!!ALOMWEEEEEEEEEEEEEEEEEE THATS WHAT YOU ARE KNOWN FOR

 241. fodya says:

  mpaka kusinzinira maso mix sound oooooh koma ndi ayaaya yayayayaaaya

 242. sinthole,manondo,mphwiyo,lutepo says:

  alomwe alomwe nopiya!

 243. YOLANDA says:

  koma ana amlakho kuyaluka abale,angonife ndi achewa timakhala bize ndi zinthu zothandiza mabanja athu.

  kwanu maliro,kwathu maliro,kufera komwe anachokera.shaaaaaaaaaaa.abusa anu ndani angodalitsa.analibenso ndalama uyu zokalipira room,taonani phokonyoreyo,chiphapha cha galimoto lakelo

 244. Rose foloko says:

  Azimayi anzanga mwayamba kumafuwula ngati azungu muzigwidatu! pamafuna kachetechete.

 245. jendake says:

  Palichani apa, muwonere bluemovie yathuyathu ya kwa Jenda

 246. Mwana says:

  Koma olo ine chimkazi chimenechi ndingachidye plain ,chili mbeeee kuyera.chingakome chimenchi bwanji,aise olo akuchose ntchito zako wadya kale

 247. YOLANDA says:

  koma ana amlakho kuyaluka abale,angonife ndi achewa timakhala bize ndi zinthu zothandiza mabanja athu.

  kwanu maliro,kwathu maliro,kufera komwe anachokera.shaaaaaaaaaaa.abusa anu ndani angodalitsa.

 248. yesaya phiri says:

  zinthuzi zikumafunika chonchi mgalimoto, ndimomwe zimabeba ntchito za manja a munthu wammuna zizichitira umboni

 249. Ndadya Zanga says:

  Nawenso Guard umafunapo chani. Ukanawasiya anzako amvane kukoma. Jealousy. Iwe mfiti eti?

 250. Gilbert Ntweya says:

  kkkkkkkkkkkkkkkkkk palibe po kanthu apa.akuphunzira amaenewa,ya mu galimoto imakoma kwambiri koma sifunika phokoso olo ukhale kuti sudalowese bwino,mkaziyo azipilira basi

 251. Emmatuwa says:

  bwanawe wadyeratu zako pamenepa chikazi chooneka chabwino ayi takutaira mtengo
  ma auditor nonse ntchito mukakhala kuntchito m’matero yeti ndinu zitsiru za anthu.
  bwerani kwathu kuli malo aulele.

 252. nyenga says:

  missed opportunity was not to pay the guard a little something…eeeeish zoti panatchenedwa apa ndakayika

 253. anabel mitawa says:

  alomwe woyeeee

 254. Achalume says:

  Vuto lofuwula popanga sex ndilimeneli!Pamafunika cold war!

 255. Nyamalikiti says:

  Iwe zoona osamuthyula guard kuti umenye machine mwamtendele. Unakafunsa ife mafana apa bwandilo mmene timapangila, ma guard safuna zambili k200 basi, chitetezo 100 percent, unayitayila pamenepo game.

 256. Charger cha mutu waung'ono says:

  Koma ndiye wamudzala nayotu…akuchita kuyililira

 257. Emmatuwa says:

  Awa si anthu koma agalu chigololo chanji chochitira Mgalimoto munthu wa ndalama ngat uyo kuumiratu kumeneko taona wayaluka makolo anu akuti chiani akaona zimenezi,ha ha ha ha ha chigololo ndichabwino yeti

 258. PP says:

  Mwati ndiwaku Thyolo????????????????????????????

 259. PLEASE NYASA TAKE THE PICTURE AWAY, TIME OF KAMUZU THIS COULD NOT EVEN APPEAR HERE.RESPECT YOUR BODIES GO TO THE HOTELS/LODGES,FOR PRIVATE MATTERS.

  1. Malawiana says:

   Whats wrong with the picture? Is it making you perpendicular to yourself?

 260. ezekiel Luhanga says:

  mbola

 261. envy says:

  Ma rest house onsewaaaa……. tikati lodge mwina kudula koma abale. Kuwumila kapena?

 262. mathews chilonga says:

  makolo ndi achibale aonu mukutipo bwanj.mwapanga2 history yonyasa.hahaha

 263. Palibe nkhani apa. Ife tachita kambirimbiri mu galimoto. Kungoti mfanayu alibe style. He should have paid off the night guard.

 264. mbwaxe says:

  Angulu okhaokha kudyana!!!!! Chitundu chachigololo!!!!!

 265. Manyasa says:

  ALOMWE HMMMMM

 266. Kanjex says:

  Kkkkkkkkkkk it happens

 267. Gabriel mwale says:

  Alomwe, akhokhola, angulu odya njoka awa mumayembekezera chani

 268. vin says:

  Alomwe kukonda chigololo ngati agalu a chisika. Nchifukwa chake ali mbwe ana osapita kusukulu chithandizo ayi kukula ngati agalu mopemphapempha. shit!!!

 269. Tengupenya says:

  Palibe nkhani apa. Usiku. Mugalimoto. Anabisala.

 270. Aseleka says:

  Our society is embrolled with indecent act….how can one enjoy sex whch involves private parts in an open ground like Mwaiwathu car park…azibambo okwatila ali mmavuto coz akudalila kuuti mkazi wawo ali kutchitooooooooooo uku katundu akupita

  1. Tengupenya says:

   Ziliko liko!

 271. heleba says:

  feeling feeling

 272. King Zude says:

  Awa ndiye agalu enieni,ma lodge onsewa??Paja ma guy a btz kuwumila cash,amaona kuluza kukalipira ku lodge.wayaluka ise..kkkkkkk.

 273. Den Den says:

  woza friday

 274. moyenda maulidi says:

  dziko lili manja mwa agalu

Comments are closed.