Email a copy of 'Carlsberg Cup semi-finals to be played at Kamuzu Stadium and Civo Stadium' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Carlsberg Cup semi-finals to be played at Kamuzu Stadium and Civo Stadium' to a friend
A distinguished and well known economist and academician, Prof. Benson Kandoole, passed on around noon on Tuesday at Kamuzu Central...
Sizoona
Bullets in ma mind
A FAM zitsiru za a2 Walter should step down ndamene apangisa zosezi.
Kkkkkkk inu a shocker simumadziwa za mpira,its semifinals the look on security and patronage of pipo.the spouse nawonso amafuna money mukufuna akamenyele Ku tchile ngati kumeneko anga kalipile 1000 ndindani,osadzanenaso mau amenewa anthu adzakusekani
Noma forever
Noma yanga woyeee!mabanker tili nanu
Woza!!be4 wanderers my favourite team.Fixture ili bwino kwa ife!!ma banker tili pambuyo panu!!!!
Gwaladi ndi wa Noma kuyambila kale..
Pa Carpet Nde Ma Banker Amaukatu, Bb Mukathamangitsdwa Molapitsa Pa Kamuzu Stadium Tikupezani Konko Kaya Akubelekani Kaya Ayi Ife Tikubwera Konko Koma Why Nama Vs Kaning’ina Lions Playing At A Neutral Venue? Asiyeni Akamenyele Ku Mzuzu Or Ku Bt Otherwise The Match Is Being Fixed, Apapa Mukukokela Noma Ndi BB, Mukiyendetsa Silva Komaso Moyale Ndi Cholinga Pamene Noma Mwangoibweletsa Ku LL Chiphamaso Mukuziwa Chomwe Mukupanga Osatipusitsapo Apa Komabe Tikamenya Bola Mwaziwa Kuti Mwatchela
FAM and Carlsberg mwakhwana heavy. Ife tufuna Bullets v Wanderers in final. Its very obvious if Wanderers would hav lost to Moyale if the game was to be played in Mzuzu and similarly Silver would have whipped Bullets if the game were played in Lilongwe.