Email a copy of 'Carlsberg Malawi raises prices of beer, soft drinks' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Carlsberg Malawi raises prices of beer, soft drinks' to a friend
A local theatre, ‘Theatre International’ is set to premier at Golden Peacock Hotel its first film Mwayi Wotsiriza (Last Chance/Dernière...
Ife chimodzimodzi tizimwabe amene simungakwanise leave and join majilijili.com its where u belong
There should be a competition between Brewers in malawi. Invite more Brewers to open their business. Carlsberg amayenjeza kubera wanthu.
Very stupid.
Osakangochitanso deal ndi Palladin on what Malawi gets from uranium instead of raising beer prices.
And now tidzimwanso zedi akhaule ndi otolera tax sitizilipira. Shupiti.
Zanu musova guyz ife ndi amstel basi pa jozi kumeneko tixaonabe
Peter akufuna ndalama zokwelera ndege ndi anthu ake a ku ntholo
Womwa tea azamwanso!
Dulitsani surf wanuyo.Panopa tizimwa,Win,Royal Palm ndi chibuku.Khala nawoni matokoso anu odula kuposa mowa woyotanitsawo.
Kuyamba kukwera zinthu ndi lero fotseki
There is no issue here even here in South Africa from 1 Oct the beer price was up and to be frankly Carlsberg price not so bad there in Malawi.
We are in the days where a seller becames happy but a buyer weap.