Email a copy of 'Caroline Savala mute to prosecution evidence on cashgate: Sentencing adjourned' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

53 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Mafia
8 years ago

Silent means concert

zora
zora
8 years ago

Ine koma weave yo siikundibwinoyi, ikundipanga irritate.

She deserves that, ankadya okha ankatishayinila.

Paulo Mpwiyo
Paulo Mpwiyo
8 years ago

Wayamba kutuwatu. Pang’ono pang’ono mupelepeseka nonse.

Mkamwiniwakwata
Mkamwiniwakwata
8 years ago

A Mkondiwa pali magalimoto ena a boma ali ndi ma private number upeza lero akuyendetsa akazi a bwana ulendo ku shower mawa ndi a bwana kupita ku bwandilo or kuchiztemba kukasisila, koma ena akumakhala ma Tax usiku sinditchula magalimoto ake koma fufuzani muwapeza.

Lorry zaboma zikunyamula mchenga, njera, matabwa ngati za hire, zikuchitika mu civil service yanu. Kodi kale magalimoto amasungidwa ku office pano munasiyilanji? Every two months galimoto kugarage ndi zoona zimenezi, kodi ndiye civil service ingatukuke chonchi? ayi zanyanya. Tikonzeleni zanyanya.

Mkamwiniwakwata
Mkamwiniwakwata
8 years ago

Zoona anthu ambiri timaba munjira zosiyana siyana kungoti la 39 silinakwane mwachitsanzo kuchipatala mankhwala, ku education chalk, duster, mabook, ku agriculture fertilizer wa subsiday, ku police kulipilitsa belo la ulele, immigration kudisha ati passport permit ituluke msanga, mu other government ministries mai amaonjezela mitengo kugarage, stationery suppliers cheque chikatuluka kukagawana, ena maallowance opanda kupita kufield ma civil servants akulandiral ena 20 nights imagine. Upeza bwana wao amene amayenda naye ali ndi ma night awiri koma bridal party 10 kapena 15 nights sikuba kumeneku. A Chilima ndi Mkondiwa zikuchitika mwezi ndi mwezi mu civil service yanu inu muli busy kupanga draft… Read more »

peeping lizard
peeping lizard
8 years ago

kodi bwanji milandu yonseyi maminister of finance ,from bingu to abiti sakutchulidwa ndekuti samaiona cash gateyo.malawi wambalazokhazokha

maxolomeo
maxolomeo
8 years ago

prison monger dont insult my intelligence,r u serious of wat u r sayin?

Robs
Robs
8 years ago

Mkaziyu anaba koma ndi bed material

Half Mkango
Half Mkango
8 years ago

“Be compationate with sinners”

chidongo John
8 years ago

Zimaweevezo a Malawi zikunyasa angakhale kuno Ku Joni ayamba kudanazo amuna amene mukuti mukukopawo akumayankhula tsiku ndi tsiku pa ma phoning in programmes kuti zikuwanyasa ndipo ndi azimai wochepa amene akupanga zomenezo kuno Ku Joni masiku ano. Ndivomerezane naye wina wanena kale uja. Amuna sitifuna ma weeve, Zara kapena titi zikhadabo, sidze za fake ndiponso kunenepa ngati nkhumba. Mukusoweka kudzikhulupirira pa inu nokha kuti ndinu wokongola ndi mpaka kufuna kuoneka ngati mwenye kapena nzungu pr kupikisana ndimahuleko kuti asakulandeni amuna ndiye ayi. Mukakwatiwa ulesi kungoti mpwii kumangonenepa ngati nkhumba kakaye kubereka mwana woyamba nkhalamba zenizeni ndi stress opandanso jogging ndiye… Read more »

Read previous post:
China gives Malawi K17bn grant for Police, Community Colleges: Benefits of ‘Look East’ policy

The Chinese government has granted Malawi K17 billion to go towards procurement of Police Service vehicles and establishment of community...

Close