Email a copy of 'Cashgate: Court to rule Dzinyemba Soko 'appeal' on conviction, sentence' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Cashgate: Court to rule Dzinyemba Soko 'appeal' on conviction, sentence' to a friend
Former President Joyce Banda said she will be returning back home in October but the month ends this weekend with...
Achepetsereni zaka ndi theka abwanawo azaone abale awo.
Kodi Jesse Kabwira paja amati a MCP saba. Tsono mmesa anali member wa NEC and National Deputy Director of Youth mu Committee ya Chakwera. Kanthu ako!!!
tikuvutika chifukwa chambalame ngati zimenezi, rot in jail
Appealing on a fair penalty!
Si mtumbuka uyu!!!!! Koma atumbuka!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!
THE COURT SHOULD ALSO CONSIDER THAT BECAUSE OF HIS CORRUPTION HOW MANY MALAWIANS HAVE SUFFERED AND SOME HAVE ALSO DIED OTHER LIVES HAVE BEEN DESTROYED. IF I WAS A JUDGE I WOULD SENTENCE HIM LIFE IN PRISON.
Soko sumadya ndalama zaCashagate ndimahule kwaBiwi ndikukuuza siyanani nazo ablazi zimenezo. Mwagula ma mini bus heee kumanga garage lelo muziti appeal. Inutu khalani konko tiwonana 2021!
PVHO ndi Stecelia anyamuka liti?
Lero nde zikuwawa pamene nthawi yomwe mumaba zimakoma kumatishayinila a Malawi kuti ndinu opeza bwino zili zakuba. Fotseki
PVHO ndi Stecelia motors muwanyamula liti?
Wakuba ameneyo. Nanga william kachingwe mumutenga liti?