Email a copy of 'Catholic Bishops start solidarity visits to flood victims in Malawi' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Catholic Bishops start solidarity visits to flood victims in Malawi' to a friend
Mighty Be Forward Wanderers on Monday buried the bitter rivalry with Big Bullets when they donated K200,000 (US$444) to Malawi...
Keep it up and may the almighty Holly Father keep on blessing his church
Koma akatolika otchuka mu ntchito zawo alipo pa malawi. Raphael kasambala, paul mphwiyo, thereza namathanga senzani, mwa ena. Sithole naye ayenela kukhal mukatolika malingana ndikuti Mchinji ndi ku chimake cha katolika.
A tear of Joy stands in my eye. . . . . .
Zikomo kwambiri kwa akristu nonse Akatolika popereka nsembeyi. May the Almighty God
bless you.
Mpingo woyera,wapamalo ponse, wofumira kwa apostoli. Nthawi ino yokumbukira kuzunzika ndi imfa ya Ambuye Yesu pamtanda, chitani ntchito zachifundo – kupemphelera, kuyendera, kudyetsa ndi kuveka anzathu ovutika ndi madzi osefukira mdziko muno. Ambuye azikudalitsani nthawi zonse atumiki a Mulungu!
Mpingo wa pamalo ponse wofumira kwa apositoli, womwe ukusunga manda a POPE woyamba Simon Petulo ku Vatican. Unamanga ma sukulu ponse ponse, unamanga zipatala ponse ponse, umalangiza boma kuti liziyenda bwino osamangosokosa zopanda nzeru ai. Komanso boma likamapanga zachibwana umalemba ma pastoral letter osati amasewera ai. Lero mpingowu wayamba ulendo wodyesa nkhosa za ambuye zomwe zavutika ndi madzi. Bravo catholic, bravo akrisitu ndi ena akufuna kwabwino omwe anasonkha nawo billion kwacha imeneyi. bravo boma polola ufulu wa chipembezo.
Yes, holistic approach of Jesus Ministry. You are setting a good example.
GOOD JOB AUNCLE
Eeeeeeee, khristu
Osangopita kothandizako bwanji mpaka kulengeza. Pochita ntchito za chifundo chimene dzanja lako la manja lichita chisadziwike ndi lamanzere.