Email a copy of 'CCJP urges Malawi citizens to come back home: Back protests at South Africa embassy' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

28 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
golden eye
golden eye
9 years ago

AFRICA UNITE anayimba BOB Marley for the sake of the continent. Ulosi unachitika apa ankaziwa kuti anthu ena ndi osokoneza. First of all let me grieve with all affected… sorry for the attacks but GOD is good all the time, you have come back and alive. what is more important is your life. MOYO NDI MPAMBA…There is a lot back here home you can be doing. After confronting and disgracing you need to bury the hatchet and move forward as people who are responsible. Ndinu anthu olimbikira ndichifukwa chake anzanu a ku Joniko amapanga nsanje… mutati luso lomwe limapangitsa anzanu… Read more »

mbani
9 years ago

Apitanso madzulo ake ma passport abisa kale adya chani ku Mzimba and Mangochi. Chamba and Bonya?

petro
9 years ago

Nzeru zikachepa, sibwino kumapeleka ma comment, chifukwa mumapeleka ma comment opusa. Siyani anthi a nzeru akambilane.

ELECTORATE MZIKA
9 years ago

Mr Chisoni ndi CCJP Yanuo mind your tongue.Dyera basi!Mukungofuna mutamikirepo kuti mmatha kulankhula?Za ziii! Kodi CCJP yanuyo yachitapo chiyani kwa anthu okhudzidwawo chikhalirecho ndi Mulhakho wanuwo mukungosekelera mapulezidenti ndi andale akubela aMalawi.Anthu kupita kunjaku nkufuna kudzidalira.Chilungamo ndi mtenderezo zilikuti?Dzingodyani za Aromazo.Koma kunsewu kwanuko ndi Billy’yo musamaleko.Anthu amene ali ku RSA sikuti ndiwopusa iyayi.Pro-active action is what we need and not malangizo opusa ayi.

Kelly
Kelly
9 years ago

It is sad to learn how our fellow Africans are being treated in South Africa. We Malawians we are so timid to continue buying from shoprite and Game whilst the owners of these shops are harasing our people in their country. Even the salaries they pay our people in shoprite, peanuts! K23000 (500Rands) can they pay that amount of money in RSA? I don’t think so. Anthu awa akulemerera paife koma nkumachitanso mwano. tiwakhaulitsenso adziwe kuti south africa is not superior on its own, we are contributing to their economy and superiority. Its high time they learn to appreciate others.

chigoli
chigoli
9 years ago

Koma enanu mukuti bomali likulephera ndicho chiifukwa anthu akubwera ku Joni kuno?
Bodza,osati ili ayi, koma boma la MCP linalephera kumanga madziko oyenerera a dziko lathulo ndicho chifukwa zipani zina zikuvutika pano.
MCP go to hell. Kamuzu wanu anatinena ife akumpoto kuti, “WE ARE DEAD NORTH.”

precious
9 years ago

Malawi should address it’s own xenophobia first because we don’t have moral authority to judge others. You can’t remove a speck in you neighbor s eye when you have a spec in your own. Mr chisoni please star complaining against the tribalism and nepotism happening in Malawi then you shall receive credit for what you are saying.

S B
S B
9 years ago

Eeee iwe khala nchete, ife sitingabwele kumeneko, better to die here than to com there, tizabwel tikafona osati zotiyitana, u cant afford use com there to do what? mwayamba kusuta fodya wakulu!

ujeni
9 years ago

We have no working government thus why people go to do labour jobs in other African countries. We should be ashamed of ourselves for failing to create jobs even street sweeping, road construction. All we have done for the past 50 years is hero worshipping a president.

Gladwell
Gladwell
9 years ago

Mr Chisoni mukundivetsa Chisoni ndizokamba zanu.Kodi tikabwera kumeneko mudzatilemba ntchito tonse or we wil b ur roughing stocks?

Wailing Soul
Wailing Soul
9 years ago
Reply to  Gladwell

For sure, no wonder you will be stuck in SA. No one can employ you here with such English as “roughing stocks”kkkkkkkkkk

Read previous post:
Bullets title defence off to perfect start: Malawi TNM Super League

Big Bullets title defence got off to a winning start with a 2-1 victory over Silver Strikers on Saturday in Lilongwe with goals by...

Close