Email a copy of 'Centre for Social Concern asks Malawi govt to regulate tenancy labour system' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Centre for Social Concern asks Malawi govt to regulate tenancy labour system' to a friend
Weddings are times of joy, and when wedding invitations are sent, the host or hostesses expect the people who are...
When individual interests block progress for the country, typical case example. ECAM led the finalization of the Tenancy Labour Bill by tripartite social partners which the Ministry is happily sitting on.
Comment:dziko langa!
Bvuto apa ndi kusowa kwa ntchito.Ku siya utenati zinthu zingabvute kosekose.Anthu angafe ndi njala,fudya uzakhala ochepa,boma ndalama zakunja zizachepa ndipo uphawi uzakula
john chilembwe adafa pofuna kuthetsa thangata lomwe boma likulimbikitsa leroli,boma livomera bwanji kuti munthu agwire ntchito kwa chaka chonse ndiye adzapatsidwe ndalama. Mudaona malo, nyumba, madzi ndi chakudya cha matenant, kuti tili ndi omenyera maufulu a wanthu, ma donors okha ndiye akudziwa chifukwa amapereka ndalama zawo, ndakaika ngati mchitidwe wa utenant umalimbikitsa maphunziro a wana. Alomwe enanso ndi matenant ngakhale apulezident mukingopenya
Exploitation goes beyond tenants it is every where in the labour market including civil service, domestic helpers, salesmen in indian shops, police, etc
Ife tikufuna matenanti akumwera kuno ku Kasungu makamaka alhomwe.
TAYESESANI MUTHESE THANGATA