Email a copy of 'Chakwera holds MCP shadow cabinet meeting: Discuss Malawi situation' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Chakwera holds MCP shadow cabinet meeting: Discuss Malawi situation' to a friend
The Consumers Association of Malawi (Cama) has condemned the xenophobic attacks of foreigners in South Africa including Malawians and has...
Ok
Mtima suvala sanza
Ine ndikayankhulapo mumva eeh amakonda kwambiri apm ndiye chabwino tizisiye choncho sindilankhulapo kanthu paja ine siwandale
My beloved party
Kkkkkk! Wonders will never end. Tiyeni nazoni za u shadowzo
Vuto lathu ndi limeneli a Malawi kuvetsetsa zinthu kumativuta. Yanenedwa kuti shadow cabinet potengera anthu omwe alipo panopa munchipanimo. Mesa paja awiri sangayende limodzi asanapangane NDE anthu enawo kaya akumpoto kapena kumwera ayikidwamo bwanji poti ambiri mwa Iwo kamba ka dyera ndi kudzinva kaya kudzikonda ali otangwanika kufunafuna mpando kwa a pulezident a panowa. Koma akunama kuti afuna athandize boma mapulani NDE a Malawi tikufuna zomwezo tidzingonamizidyabe basis.. Chifukwa cha anthu ochepa ozindikira mwa umbuli ife mbuli kalefe tidzingotsatira poti tonse khungu likutivuta.. Kod munthu wosamudziwa ungachite naye zinthu zofanana..????
DPP ndi dilluuuuuu
Majoti will remain a life supporter of tha nyau party. Being one of the kangw’ingw’is gologolos will remain like that for life. Now that the party is being led by commander in chief of gule wamkulu, Lazaro. Tasiyani kuzipaka manyi kukamwa abale. Musamasanduke virombo muli anthu.
My Party For Life. Osati Nkhalamba Yopanda Mano Mkamwa, Kumangotafuna Lilime Nthawi Zonse!
mcp ndi yongoyerekeza mpaka kale, anthu akulu akulu nkumachita zongoyerekeza pali nzeru apa?