Email a copy of 'Chakwera walks last born daughter down the aisle' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Chakwera walks last born daughter down the aisle' to a friend
When people are desperately in need of something, they usually refer to a statement which says that half a loaf...
no parent wishes his children to misbehave and to attack other leaders just becoz yours is married is useless what if she were married to Obama mukanatukwana mtembo unfortunatel ndi mavenda azanthu omwewa and she is not the best out there
Musayambe kumunamizira Malryn che Nathan. Ngati mumamufuna mukanangonena kuti mwachedwa kufunsira. Mumachedwa ndi bowa bwanga. Wapita basi ngakhale munene zofuna kusokoneza zakuvutani.
Watichotsa manyazi tonse akhirisitu zikadakhala kuipa tonse tikadachita manyazi ‘pajatu amati ikaola imodzi zaolazonse’ Thank You Dr. Rev
Zauchitsiru izi basi.Dont say Munthu wa Mulungu coz adathetsa ubale ndi Mulungu.
my friend, dont wary. It happens kwa an2 ambiri so just 4get her and start new lyf. Let her stay peacefully in her just wedded family. Be a man please!!!! Dont curse her ever bt wish her good things
Aaaa Malryn, wakwatiwadi iwe, ine kundisiya pa dzuwa! Paja tinapangana kuti tikwatirana pa 25 December tu! Poti tsopano ndiwe mwana wa Purenzidenti wa MCP ndi mtsogoleri wa Otsutsa Boma basi wayamba kundigenda ndi miyala!
Za ukwati zomwezi, zokamba, “mbweee!” Manyazinso mulibe. Kaduka basi. Mukhalira zomwezo, anzanu akupita patsogolo.
well done chakwera we adore u
None of our business, ma ukwati ena anachita tsiku limeneli osalemba pa nyasapa bwanji ?za ziiii anthu akukwatilana everyday, m’ma midzimu.
kulera kwabwino, congrats