Email a copy of 'Chande final determination ready by Sunday – FA Malawi' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Chande final determination ready by Sunday – FA Malawi' to a friend
Government has committed itself to honour its outstanding debt of around MK7.5 billion to the Central Medical Stores Trust (CMST)...
Ameyo noma itenge
B B Ndiyolakwa; SULUMBA; KUMWENDA apita ku bb noma sidawaopyese
Tango wawuzani zenizeni anthu inu a FAM. zatitopetsa izi
BFW ndi ya F A m , Sapota wamkulu wa BFW ndi Sulom. A Fa tangogamulani nkhaniyo panja tidziwa kale munakanika kulongosola Fam election saga, nkhani ya Dedza mulepheranso , Malayisesi mwalepheranso mwangozisiya mumalere, Ndiye nkhani ya Chande mugayithe mwachilungamo? IF That, It will be the First in this Current reign of Fam and sulom. what we want is chilungamo Kaya ndi BB kaya Chande kaya ndi BFW chilungamo chioneke.
Ameneyo ndi wa Noma basi