Email a copy of 'Chewa Heriage responds to Kabwila appeal for Malawi flood disaster' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

26 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
prince
prince
8 years ago

Alomwe ndinu agalu abasi kadzivinanu maliseche basis mbuzi

Nyau ya kudambwe
8 years ago

Namchunjule ndi nyau yowoneka bwanji? Virombo vikamakuwa osamaziyankha. MCP ndi chipani cha nyau zokhazokha. Kapena ndikunama. Ndani chewa amene sadamete. Dzikoli silingalamuli- dwe ndi virombo (nyau). Kamuzu (Richard Armstrong) adali wa ku Ghana, ndichifukwa chake adalamulira. Akadameta( akadasanduka nyau) sakanalamulira dzikoli. MCP inaba Capital city kuchokera ku Zomba, zoona zabodza?
adali wa ku Ghana

Phodogoma
Phodogoma
8 years ago

Koma Nanchunjule ungotipwetekatu ife alomwe. Ndipo mlhakho wa alomwe umakupwetekani bwanji? Jessie Kabwira siuyu akulimbikitsa chikhalidwe cha Gule wa Mkulu. Ndipo ife a Lhomwe sitikuona vuto. Koma zikakhala za ife a Lhomwe a Chewa mumachita kutsegula m’mimba. Mavuto anu ndi angati a garu inu. Mumuuze Chakwera kuti sadzalamuliratu dziko la Malawi. Ngati ndi Profeti Sinodeni amene adamunamidza kuti dzikoli likufunika born again, ndiye born again si ameneyu. Mu

sbobet
8 years ago

thank you

Kaidi
Kaidi
8 years ago

Chonde musadane ndi alomwe

wamasomphenya
wamasomphenya
8 years ago

Kodi galu ndani mmalawi muno yemwevsadziwa kuti palibe chisankho chomwe dpp idawinapo?? Zonse kubera. Likudza tsiku lowawitsa kumene momwe a dpp ndi UDF mudzalila ndikukuta mano Ambuye Yesu atayika pambalambanda machismo any, pitala wanu akutsegulilidwa khomo lajahena tsiku kumeneko mudzalila ndikudziguguda pamtima mukunena kuti if only we played it fair but alas it will be too late

PATALI
PATALI
8 years ago

Mantha a lomwe. Tokotani mumveke ndinthu

Mlomwe wa Alhomwe
8 years ago

Kodi nonse mukuti nyo nyo kulimbana ndi Alhomwe’fe, why are you doing this? Ife Alhomwe timakuchimwirani chiyani abale? Tiwonana 2019 agaru inu! Ngati pulezidenti achokere from centre ndiye kuti mwalemba m’madzi. Remember that Chakwera wanted to woo Christians to vote for him. Kodi Chakwera wanuyo anaiwona vote? Kodi aliponso wina woposa APM kumbali ya ndale? APM woyeee! DPP woyee!

Mayi a Buledi
8 years ago

Dogs

God's Favour Ministries.
God's Favour Ministries.
8 years ago

Achewa musamadzinamize kuti mcp idzalamulanso maloto a chumba amenewo,kodi munatuluka liti m’boma.
Ndiye akabwira kuchita kuwaphatha choncho abambowo? Ee akufuna amve kutenthatu.

Jose'
Jose'
8 years ago

All this noise for donating 1million? $2000? Putting btogether resources from the USA? kkkkkk Achewa chimene mumatha nkudzipaka matope ndi bibi kukamwa mwati nde gule

Read previous post:
Key state witness risks perjury charges, lied on Kumwembe conviction: Mphwiyo’s case

A case involving former minister of Justice Ralph Kasambara and others who are accused of the attempted assassination of former...

Close