Email a copy of 'Chief arrested over ghost workers in Karonga MASAF program' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Chief arrested over ghost workers in Karonga MASAF program' to a friend
A Police officer Clever Mtengerenji has been found guilty of sexual activity with a girl aged 12 The Rumphi Magistrate...
Let Him receive what he soul.
Go to mzimba n arrest stupid leaders as well (selfish people)
Nosense police take ur responsibility
Izi boma lizione bwino chifukwa zikuchitika m’boma pafupifupi lililonse anthu osauka kudyeredwa masuku pamutu.Corruption yavuta ku Malawi.Amangidwe basi akuononga dziko mbava zimenezi.
Watamya apa tata.
Akwizingidwe basi, ena atengelepo phunzilo, cashgate ndikumuzi komwe!!!
This is the only language the so-called traditional leaders understand better.
Go to salima pls now. Go trace anthu amene anagwira nchito eeeee. On the day make it public and zikakhale pabwalo anthu akuona ndikumawafusa ngati mainawo akawazindikire. Ma project ankhalangoso eeeeee onama okhaokhaaa ena pa ground palibe
Zimenezi zikuchitika pena pali ponse mdziko lino, anthu ena omwe akumagwira ntchitozi siosauka ayi, osauka akungasaukirasaukirabe.
zovuta