Email a copy of 'Chilima attends Mulli memorial: ‘No lazy bones for Malawi to develop’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Chilima attends Mulli memorial: ‘No lazy bones for Malawi to develop’' to a friend
Malawi Immigration Department says in the year 2014 the department has collected revenues of close to K3.5 billion, a figure...
Chondidabwitsa Ine nchakuti vaisi pulezidenti akukatani kumaliro a business man? Just politics as usual. President and vice president of Malawi should not be at kulonga ufumu and or kumaliro a businessman. They may as well be at a nurse’s funeral.. at least a nurse saves lives.
Zimenezi Saulos muziwuuzana ndi mzako Mbendera who was crying like baby the midst of night for betraying malawians.We r not that gullible to take everything from you.Tamangolilani Maliro a Mulli osati kuchulutsa zoyankhula zopanda pache.
Nzako zimenezo khala chocho ukudandaula pakana Yesu azakupeza kom amzako akulamula. Kodi chipani chako ndi chiti, cha atumbukachi,kapena cha nyau chi
Saulos when are you becoming Paulo? You need conversion osati zotinamiza za DPP CHIEF “WELL WISHER” MULLI.
Iwe mbuzi eti
15,000 ake ati mulli bodza. Unachotsa anthu ambili ntchito opanda malipilo. For saulos u rigged elections thru mec guys who were changing figures. We can expose u
mulinso ndikachiyani
Ma dreams a Malawi akakhoza ka MCE/Diploma ndikupeza ntchito M’boma pa Company/NGO/ ndicholinga chakuti adzipanga Cashgate
Amalawi ndi ntchamba zawanthu-tindalama takubato amangotheraso mowa ndi ma Hule pamene ana kunyumba akusowa ma basic needs
Amalawi ndi business ndikumanzere_shame!
Initially it was hard work. Then his siblings missed the path and diployed greediness & nastiness strategy.
Nobody can deny the fact that Mulli was a hard worker. But these ones heaven knows.
Mwayamba kumuyndikilaso mufuna ayambeso kusokoneza zinthu pa malawi pano? asekese ma business a amwenye, aqmangise anthu mopanda umboni, achosese apolice ntchito popanda nkhani iliyonse? zisilu inu!!!!!!!! ndiyesotu bola JBtu anamukozela mukamwa ameneyi.
i indeed wish this was the spirit. it begins at home and flourish. if people in families were that united together we would have achieved more. koma timanyozana pachibale.bravo the mulli brothers. do u not have sisters?